Mankhwala a HIV ndi EDZI - PIH Model Online - Partners in Health

Mankhwala a HIV ndi EDZI - PIH Model Online - Partners in Health Mankhwala a HIV ndi EDZI - PIH Model Online - Partners in Health

model.pih.org
from model.pih.org More from this publisher
14.12.2012 Views

136 Mutu 5: Mankhwala a HIV ndi EDZI Mutu Mwachidule Ntchito Zoti Ziphunzitsidwe Njira Nthawi Zipangizo Zofunikira 1 Mphunzitsi 2 Ali afotokoza mfundo zokhudza ma-ARV, zizindikiro zimene zili pa makhadi olandilira mankhwala ndi kumwa mankhwala mosadukizadukiza.. awiriawiri, ophunzirawa apeza njira zothetsera mavuto akumwa mankhwala modukizadukiza omwe angathe kuchitika. Kufotokoza kwa Mphunzitsi Zokambirana za M’magulu Akuluakulu Kuthandizana Anthu Awiriawiri Mfundo Zikuluzikulu 60 Minutes 40 Minutes • Matchati kapena kudzera pa makina a kompyuta • Chipangizo chotulutsa mawu ndi zithunzi (ngati akugwiritsa ntchito kompyuta) • Makhadi olandirira mankhwala • Mankhwala a ma-ARV • Bukhu la Wazaumoyo wa M’mudzi • Makhadi olandirira mankhwala • Ziyelekezo (ikatha ntchito iyi) • Bukhu la Wazaumoyo wa M’mudzi • Ma-ARV amagwira ntchito yoletsa kachirombo ka HIV kuti kasaswane m’thupi. • Munthu amamwa ma-ARV moyo wake onse. • Anthu amene ali ndi kachirombo ka HIV/EDZI afunika kumwa ma-ARV pa nthawi yomweyoyomweyo tsiku lililonse motsatira malangizo ake. • N’zovuta kumwa ma-ARV tsiku ndi tsiku kwa moyo wonse, koma ngati anthu amene ali ndi HIV/EDZI adukiza kumwa mankhwala, ndiye kuti mankhwalawo sagwiranso ntchito. • Ngati odwala amwa mowa kapena mankhwala osokoneza bongo zimachititsa kuti ma-ARV asamagwire bwino ntchito mthupi. Bukhu Lophunzitsira Alangizi Azaumoyo a M’mudzi a Bungwe la Abwenzi Pa Za Umoyo: Chisindikizo Choyeserera

Ntchito 1 Mankhwala a ma-ARV Kufotokoza kwa Mphunzitsi Zokambirana za M’magulu Akuluakulu Nthawi 60 Minutes Zolinga Mutu 5: Mankhwala a HIV ndi EDZI a Kufotokoza kuti mankhwala a ma-ARV amagwira ntchito yoletsa kachirombo ka HIV kuti kasapitirire kuswana m’thupi. b Kufotokoza nthawi yomwe ma-ARV ayenera kumwedwa, kangati pa tsiku, kwa nthawi yaitali bwanji komanso kuchuluka kwake. c Kudziwa mayina a ma-ARV ndi zizindikiro za mankhwalawa zomwe zimagwiritsidwa ntchito pa makhadi olandirira mankhwala. d Kufotokoza kuti ma-ARV amafunika kuwasunga pamalo ouma, osawala dzuwa, ozizirira komanso oti ana sangawafikire. Kukonzekera • Sonkhanitsani mankhwala a ma-ARV osiyanasiyana ndi moti muikemo mankhwalawa monga mabokosi kapena mbale. • Konzani malo osachepera asanu m’chipindamo kuti pamalo alionse pakhale anthu asanu kapena ochepera apa. Ikani mankhwala ndi makhadi olandirira mankhwala pa malo alionse. • • • Zipangizo Zofunikira Matchati kapena kudzera pa makina a kompyuta Chipangizo chotulutsa mawu ndi zithunzi (ngati akugwiritsa ntchito kompyuta) Makhadi olandirira mankhwala • Mankhwala a ma-ARV • Bukhu la Wazaumoyo wa M’mudzi Bukhu Lophunzitsira Alangizi Azaumoyo a M’mudzi a Bungwe la Abwenzi Pa Za Umoyo: Chisindikizo Choyeserera 137

Ntchito 1

Mankhwala a ma-ARV

Kufotokoza kwa Mphunzitsi

Zokambirana za M’magulu Akuluakulu

Nthawi

60 Minutes

Zolinga

Mutu 5: Mankhwala a HIV ndi EDZI

a Kufotokoza kuti mankhwala a ma-ARV amagwira ntchito yoletsa kachirombo

ka HIV kuti kasapitirire kuswana m’thupi.

b Kufotokoza nthawi yomwe ma-ARV ayenera kumwedwa, kangati pa tsiku,

kwa nthawi yaitali bwanji komanso kuchuluka kwake.

c Kudziwa mayina a ma-ARV ndi zizindikiro za mankhwalawa zomwe

zimagwiritsidwa ntchito pa makhadi olandirira mankhwala.

d Kufotokoza kuti ma-ARV amafunika kuwasunga pamalo ouma, osawala dzuwa,

ozizirira komanso oti ana sangawafikire.

Kukonzekera

• Sonkhanitsani mankhwala a ma-ARV osiyanasiyana ndi moti muikemo

mankhwalawa monga mabokosi kapena mbale.

• Konzani malo osachepera asanu m’chipindamo kuti pamalo alionse pakhale

anthu asanu kapena ochepera apa. Ikani mankhwala ndi makhadi olandirira

mankhwala pa malo alionse.

Zipangizo Zofunikira

Matchati kapena kudzera pa makina a kompyuta

Chipangizo chotulutsa mawu ndi zithunzi (ngati akugwiritsa ntchito kompyuta)

Makhadi olandirira mankhwala

• Mankhwala a ma-ARV

Bukhu la Wazaumoyo wa M’mudzi

Bukhu Lophunzitsira Alangizi Azaumoyo a M’mudzi a Bungwe la Abwenzi Pa Za Umoyo: Chisindikizo Choyeserera 137

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!