Mankhwala a HIV ndi EDZI - PIH Model Online - Partners in Health

Mankhwala a HIV ndi EDZI - PIH Model Online - Partners in Health Mankhwala a HIV ndi EDZI - PIH Model Online - Partners in Health

model.pih.org
from model.pih.org More from this publisher
14.12.2012 Views

158 Mutu 5: Mankhwala a HIV ndi EDZI Zomwe Wazaumoyo wa M’mudzi Ayenera Kukumbukira Kukawatengera odwala mankhwala ku chipatala mwenzi ulionse. Kupita ndi wodwala kuchipatala mwezi uliwonse kukatenga mankhwala. Kuonetsetsa kuti odwala akusunga mankhwalawo pamalo otetezeka, ouma, osawalira dzuwa komanso oti ana sangafikire Kuonetsetsa kuti odwala akulandira ma-ARV a mtundu woyenera. Kuonetsetsa kuti odwala akumwa ma-ARV awo moyenera. Kupenyetsetsa odwala kuti aone zizindikiro zoti sakutsatira makhalidwe abwino owathandiza kuti akhale ndi moyo wathanzi ndi kuwapatsa uphungu kapena kuwatumiza kuchipatala ngati nkofunika kutero. Bukhu Lophunzitsira Alangizi Azaumoyo a M’mudzi a Bungwe la Abwenzi Pa Za Umoyo: Chisindikizo Choyeserera

Zolembalemba Bukhu Lophunzitsira Alangizi Azaumoyo a M’mudzi a Bungwe la Abwenzi Pa Za Umoyo: Chisindikizo Choyeserera 159

158

Mutu 5: Mankhwala a HIV ndi EDZI

Zomwe Wazaumoyo wa M’mudzi

Ayenera Kukumbukira

Kukawatengera odwala mankhwala ku chipatala mwenzi ulionse.

Kupita ndi wodwala kuchipatala mwezi uliwonse kukatenga mankhwala.

Kuonetsetsa kuti odwala akusunga mankhwalawo pamalo otetezeka, ouma,

osawalira dzuwa komanso oti ana sangafikire

Kuonetsetsa kuti odwala akulandira ma-ARV a mtundu woyenera.

Kuonetsetsa kuti odwala akumwa ma-ARV awo moyenera.

Kupenyetsetsa odwala kuti aone zizindikiro zoti sakutsatira makhalidwe

abwino owathandiza kuti akhale ndi moyo wathanzi ndi kuwapatsa uphungu

kapena kuwatumiza kuchipatala ngati nkofunika kutero.

Bukhu Lophunzitsira Alangizi Azaumoyo a M’mudzi a Bungwe la Abwenzi Pa Za Umoyo: Chisindikizo Choyeserera

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!