Mankhwala a HIV ndi EDZI - PIH Model Online - Partners in Health

Mankhwala a HIV ndi EDZI - PIH Model Online - Partners in Health Mankhwala a HIV ndi EDZI - PIH Model Online - Partners in Health

model.pih.org
from model.pih.org More from this publisher
14.12.2012 Views

146 4 5 6 Mutu 5: Mankhwala a HIV ndi EDZI Werengani mafunso mokweza ndi kuwapatsa ophunzirawo mphindi ziwiri zoti akambirane awiriawiri. Akatha kukambirana funsolo uzani gulu limodzi kuti lifotokozere anzawo onse zomwe akambirana. Funsani ngati pali ena amene sakugwirizana ndi mayankho omwe anzawowo apereka. Fotokozerani ngati pali pena pamene sipanamveke bwino Pitirizani mpaka mumalize kukambirana mafunso onse. Onetsetsani kuti gulu lililonse mwalipatsa mpata wolankhulapo. Bukhu Lophunzitsira Alangizi Azaumoyo a M’mudzi a Bungwe la Abwenzi Pa Za Umoyo: Chisindikizo Choyeserera

koperani kapena dulani Mutu 5: Mankhwala a HIV ndi EDZI T30 (Triomune) Kuphatikiza mankhwala a Stavudine (d4T), Lamivudine (3TC), ndi Nevirapine (NVP) 1 pilisi (T30-d4T 30mg, 3TC-150 mg, NVP-200mg) 1 pilisi (d4T-30 mg, 3TC-150mg) Imwani kawiri patsiku: M’mawa – 6 koloko Madzulo – 6 koloko LS 30 Kuphatikiza mankhwala a d4T ndi 3TC Imwani kawiri patsiku: M’mawa – 6 koloko Madzulo – 6 koloko Bukhu Lophunzitsira Alangizi Azaumoyo a M’mudzi a Bungwe la Abwenzi Pa Za Umoyo: Chisindikizo Choyeserera 147

146

4

5

6

Mutu 5: Mankhwala a HIV ndi EDZI

Werengani mafunso mokweza ndi kuwapatsa ophunzirawo mphindi ziwiri zoti

akambirane awiriawiri.

Akatha kukambirana funsolo uzani gulu limodzi kuti lifotokozere anzawo

onse zomwe akambirana. Funsani ngati pali ena amene sakugwirizana ndi

mayankho omwe anzawowo apereka. Fotokozerani ngati pali pena pamene

sipanamveke bwino

Pitirizani mpaka mumalize kukambirana mafunso onse. Onetsetsani kuti gulu

lililonse mwalipatsa mpata wolankhulapo.

Bukhu Lophunzitsira Alangizi Azaumoyo a M’mudzi a Bungwe la Abwenzi Pa Za Umoyo: Chisindikizo Choyeserera

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!