tiyeni ticepese infa za azimai ali ndi mimba! - Planned Parenthood ...

tiyeni ticepese infa za azimai ali ndi mimba! - Planned Parenthood ... tiyeni ticepese infa za azimai ali ndi mimba! - Planned Parenthood ...

14.12.2012 Views

WHAT IS ABORTION STIGMA? KODI MANYAZI WOCOSA MIMBA NCIANI? Manyazi wocotsa mimba ndi pamene mzimai amasungidwa mosiyana ndi moyipa cifukwa anacotsapo mimba ndipo ndiwokhulupilika kukhala wonongeka. KODI NINDANI OKHUZIDWA KWAMBIRI NDI MANYAZI OCOTSA MIMBA? • Azimai amene ataya mamimba osafuna • Banja ndi ana a azimai amane acotsa mamimba osafuna. • Opereka a TOP– onse olamulidwa ndi aboza Azimai ndi azibambo amene athandiza azimai umwai wathandizo locotsa mimba Cimene mungacite; • Onse azimai ndi azibambo afunika kufunafuna uthenga pa zaumoyo wogonana ndi kabelekedwe ndi kasungidwe kuwonjezerapo njira zogwiritsa nchito kuteteza mamimba osafunika. • Anthu okhala m’malo amodzi safunika kusankhira azimai amene afuna thandizo la uthenga ndi umwai kuti ateteze kucotsa mimba kosatetezedwa. • Azimai afunika kufunafuna uthenga pamene aganizira zocotsa mimba yosafunika. SERVICE INFORMATION UTHENGA WATHANDIZO Ngati mufuna uthenga wambiri ndi thandizo pa umoyo wogonana ndi kabelekedwe kuwonjezaponso kucotsa mimba mwacitetezo conde pitani ku makiliniki awa: Mu Lusaka 1. Kiliniki la Chilanga, ku Kafue 2. Kiliniki la Chipata, mu Lusaka Mu Copperbelt 1. Kiliniki la Kawama , mu Kitwe 2. Cipatala ca Ronald Ross, ku Mufulira ndi zofunika zina za umoyo zololedwa Planned Parenthood Association of Zambia (PPAZ) P.O. Box 32221, Lusaka, Tel: +260 211 256182 Fax: + 260 211 256123, Email: ppaz@iconnect.zm Ipas Alliance Office P. O. Box 11192- 00200, Nairobi - Kenya Tel: +254 (20) 387 7239/387 0248 Fax: +254 (20) 387 6198 LET’S REDUCE MATERNAL MORTALITY! TIYENI TICEPESE INFA ZA AZIMAI ALI NDI MIMBA! Infa za azimai ali ndi mimba citanthauza kufa kwa azimai pamene ali ndi mimba cifukwa ca zocititsa zili zonse zokhuzana ndi kapena zocitisa zocokera kumimba zoyipitsitsa.. Zifukwa zenizeni za infa za azimai pobala mu zambia ndi; 1. kucotsa magazi kopitilila 2. Sepsis( Infection) 3. kuwawa kwa mimba kocingilizidwa 4. mabvuto yothamanga kwa magazi 5. kucotsa mimba kosa tetezedwa Kuteteza kucotsa mimba kosatetezedwa ndi cofunikira kwambiri ku cepetsa infa ya azimai ali ndi mimba mu zambia. Infa zocitika cifukwa cocotsa mimba kopanda citetezo zitetezedwe!

WHAT IS ABORTION STIGMA?

KODI MANYAZI WOCOSA MIMBA NCIANI?

Manyazi wocotsa mimba ndi pamene mzimai

amasungidwa mosiyana ndi moyipa cifukwa

anacotsapo mimba ndipo ndiwokhulupilika kukhala

wonongeka.

KODI NINDANI OKHUZIDWA KWAMBIRI NDI MANYAZI

OCOTSA MIMBA?

• Azimai amene ataya mamimba osafuna

• Banja ndi ana a azimai amane acotsa mamimba

osafuna.

• Opereka a TOP– onse olamulidwa ndi aboza

Azimai ndi azibambo amene athandiza azimai umwai

wathandizo locotsa mimba Cimene mungacite;

• Onse azimai ndi azibambo afunika kufunafuna

uthenga pa zaumoyo wogonana ndi kabelekedwe

ndi kasungidwe kuwonjezerapo njira zogwiritsa

nchito kuteteza mamimba osafunika.

• Anthu okhala m’malo amodzi safunika kusankhira

azimai amene afuna thandizo la uthenga ndi umwai

kuti ateteze kucotsa mimba kosatetezedwa.

• Azimai afunika kufunafuna uthenga pamene

aganizira zocotsa mimba yosafunika.

SERVICE INFORMATION

UTHENGA WATHANDIZO

Ngati mufuna uthenga wambiri ndi thandizo pa umoyo

wogonana ndi kabelekedwe kuwonjezaponso kucotsa

mimba mwacitetezo conde pitani ku makiliniki awa:

Mu Lusaka

1. Kiliniki la Chilanga, ku Kafue

2. Kiliniki la Chipata, mu Lusaka

Mu Copperbelt

1. Kiliniki la Kawama , mu Kitwe

2. Cipatala ca Ronald Ross, ku Mufulira ndi zofunika

zina za umoyo zololedwa

Planned Parenthood Association of Zambia (PPAZ)

P.O. Box 32221, Lusaka, Tel: +260 211 256182

Fax: + 260 211 256123, Email: ppaz@iconnect.zm

Ipas Alliance Office

P. O. Box 11192- 00200, Nairobi - Kenya

Tel: +254 (20) 387 7239/387 0248

Fax: +254 (20) 387 6198

LET’S REDUCE MATERNAL

MORTALITY!

TIYENI TICEPESE INFA ZA

AZIMAI ALI NDI MIMBA!

Infa za azimai ali ndi mimba citanthauza kufa kwa

azimai pamene ali ndi mimba cifukwa ca zocititsa

zili zonse zokhuzana ndi kapena zocitisa zocokera

kumimba zoyipitsitsa..

Zifukwa zenizeni za infa za azimai pobala mu

zambia ndi;

1. kucotsa magazi kopitilila

2. Sepsis( Infection)

3. kuwawa kwa mimba kocingilizidwa

4. mabvuto yothamanga kwa magazi

5. kucotsa mimba kosa tetezedwa

Kuteteza kucotsa mimba kosatetezedwa

ndi cofunikira kwambiri ku cepetsa infa ya

azimai ali ndi mimba mu zambia.

Infa zocitika cifukwa cocotsa mimba kopanda

citetezo zitetezedwe!

WHAT IS UNSAFE ABORTION?

KODI KUCOTSA MIMBA NDI CIANI?

Ku kulitsa kwa ka mwana mu mimba ka kalibe ku badwa

kunena kuti ka kalibe ku pulumuka pakekha ku bwalo

kwa mimba ya mai wake. Ici cingakhale mwazizizi

kapena kukakamizidwa. Kucotsa mimba mwacikakamizo

kuchedwanso kuti kuduliza kwa mimba

UNSAFE ABORTIONS ARE:

KUCOTSA MIMBA KOPANDA CITETEZO:

• Kopanda lamulo

• Kucitika mu malo alibe citetezo kapena malo

osasamalidwa.

• Kucitidwa ndi opereka osapita ku SUKULU LA

PAMWAMBA/ munthu osakhulupirika amenesali

katsili

• Kucitidwa ndi njira za umunthu/zosatetezedwa

• Ndi zoopsya ndipo ndizoipa ndiponso zili ndi

zobvuta zosatha musanga. Kuonjezerapo

kupwetekedwa kwa ziwalo zamkati mwa thupi.

Kutenga matenda, kucotsa magaziI kwambiri

kapena infa

WHAT IS SAFE ABORTION

KODI KUCOTSA MIMBA KOTETEZEDWA NDI CIANI?

Kucotsa mimba mwacitetezo ndi tsatilo imene

igwiridwa ndi katsiri opeleka za umoyo mu malo amene

akwaniritsa mukhalidwe wocepekela wazamankhwala.

Zitsatilo ndi njira zocotselamo mimba ndi zosabvuta

ndipo ndizotetezeka.

PROCEDURES AND TECHNIQUES FOR SAFE ABORTION

ARE SIMPLE AND SAFE

NDONDOMEKA NDI NJIRA ZINA ZOFUNIKIRA ZOCOSTSELA

MIMBA MWACITETEZO NDI ZOTETEZEKA

IS SAFE ABORTION LEGAL IN ZAMBIA?

KODI KUCOTSA MIMBA MWACITETEZO NDIKOLAMULIDWA

MU ZAMBIA?

Mu lamulo lotaya mimba lochedwa Termination of

Pregnancy Act ( TOP Act) la mu 1972, kucotsa mimba

mwacitetezo ndi kololedwa mu Zambiakulingana ndi

zocitika.

SAFE ABORTION SERVICES ARE AVAILABLE TO WOMEN

WHEN:

THANDIZO LOCOTSA MIMBA MWACITETEZO ILIPO KWA

AZIMAI NGATI:

Kupitiliza kwa mimba ku ngabweretse:

• Ciopsyezo ku umoyo wa mzimai wa mimba kapena

• Ciopsyezo cozipweteka pathupi kapena umoyo

wabwino wa maganizo a mzimai wa mimba kapena

• Ciopsyezo copweteka ana kapena kupweteka

umoyo wabwino wa maganizo ya ana alionse alipo

a mzimai wa mimba ndi cacikulu kupambana ngati

mimba inacotsedwa; kapena

• Kuti kuli ciopsyezo coyenera kuti ngati mwana

anabadwa angakhale ndi mavuto awa pathupi

kapena kubongobongo kuti angabweretse

kupunduka kwakukulu.

• Mimba inakhala cifukwa cogonewa mwacikamizo

kapena mosayenera

• Kcitidwa katswiri opeleka za umoyo.

• Mkazi apanga sankho mwamutendele kopanda

cikakamizo

SAFE TERMINATION OF PREGNANCY IS LEGAL IN

ZAMBIA WHEN:

Ngati kuli zadzidzi ndiyovomekezedwa ndi ogwira

ntchito mu cipatala atatu pamene dotolo mumodzi

afunika kukhala katswiri mu malo osankhidwawo. Dotolo

mmodzi anganene motsimikiza kwa Top ngati nicofunika

pamenepo ku pulumutsa umoyo kapena kuteteza

kudzipweteka koyipitsitsa pa umoyo wonse kuthupi

kapena umoyo wamaganizo wa mzimai wa mimba.

Cicitidwa mmalo a ukhondo, otetezedwa ndipo malo

olembetsedwa. Icitidwa ndi katswiri opereka pa zau

MYTHS AND FACTS ABOUT ABORTION

cikhulupililo: Ingati mucotsa mimba, simungakhale

ndi mimbanso (ngati cilango)

mfundo

• Kuctsa mimba motetezedwa kocokera kwaopeleka

oyenera sikuika azimai kuziopsyezo zozipweteka

kapena infa.

• Kucotsa mimba mwacitetezo sikudzaletsa kukhala

ndi mimba mutsogolo kapena kubala mwana

wathanzi.

• Ngakhale zili tero, ndicofunikira kufunsa opereka

thandizo akwanu mwamusanga ngati kuganiza

zocotsa mimba kucepetsa ziopsyezo zokhala ndi

mabvuto.

cikhulupirilo: azimuna alibemo mbali mu nkhani

yocotsa mimba– ndizokhuza azimai ndi atsikana.

mfundo

• Mwamuna ndi mukazi ali ndi danga losankha

nambala ya ana

• Azibambo nawonso ali ndi ufulu wopanga mfundo

pa zakugonana ndi kabelekedwe kamene kakhuza

azimai ndi atsikana.

• Ngakhale zili tele , maganizo otsilizila ku cotsa

mimba ali ndi mzimai.

cikhulupililo: ‘mwana’ otayiwa azasanduka cinthu

“coopsya” ndipo asayamba kubvuta mzimai ndi/

kapena banja lake.

mfundo

• ‘Mwana osabada ali mu mimba osati mwana

wakhanda’

• Azimai angakhumudwe ndi mimba yosafuna ndi

zotulukamo

• Kunyoza azimai kubweretsa kuzinyumwa ndi

kuzipatula

Cikhulupililo : kucotsa mimba ndidondomeko yo

bvuta. Simudzakwanitsa kupulumuka

mfundo

• Nthawi zina zowawa komamankhwala aliko pamene

dondomeko yacitidwa ndi katsili opereka zaumoyo.

Munthu aliyense amanva kuwawa, mosiyana-siyana.

cikhulupililo: umwai wapafupi opatsidwa wocotsa

mimba mwacitetezo

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!