Miyambo ya Anthu Mu Mpingo ya Anthu - Yesu Kristo

Miyambo ya Anthu Mu Mpingo ya Anthu - Yesu Kristo Miyambo ya Anthu Mu Mpingo ya Anthu - Yesu Kristo

yesu.kristo.com
from yesu.kristo.com More from this publisher

Monga mwa nthawi zonse ngati mufuna thandizomunjira inayiliyonse lemberani kuP.O Box 68309 Indiana Polis IN: 46268 USA,www.Yesu-Kristo.com© 1989 All at hisfeet@cs.com.Malamulo a zokopeledwa ali choncho pamene tinena za maua Mulungu ndipo tili kunena motere. Muli ololedwa kukoperapamene mwalandira chilolezo kwa eni olemba bukhuli. Bukhulindilosagulitsidwa pa mtengo wina uliwonse.Miyambo ya AnthuMu mpingo ya anthu.Kodi miyambo ya anthu yikungopezekabepamaso pa Mulungu?Chowona ndichoti miyambo imeneyi, ife tayilemekedza kwambiriyabweretsa chiwonongeko chachikulu mthupi la Yesu Khristu.Miyamboyi yachotsa utsogoleri ndi umbuye wa Yesu mpingo wakemopanda chisoni.Ndipo iye ananena nao, Yesaya ananenera bwino za inu onyenga,monga mwalembedwa, Anthu awa andilemekeza ine ndi milomoyao, koma andilambira ine kwacabe. Ndikuphunzitsa maphunzitso,malangizo a anthu. Marko 7:6 –7”Yesu yekha anapwanya nthawi yose mowoneka miyamboyao yodzidzira ndi mfundo zao podziwa kuti zitha kudzetsachitsokonedzo kwa atsogoleri ake. Chitsanzo chimodzi:Ndipo pakulankhula iye, anamuitana mfarisi kuti adye naye; ndipoanalowa naseama kudya. Ndipo anazizwa Mfarisiyo, pakuonakuti anayamba chakudya asanasambe. Koma Ambuye anati kwaiye, cikho ndi mbale, koma mkati mwanu mudzala zolanda ndizoipa. Opusa inu, kodi iye wopanga kunja kwace sanapangesomkati mwace? Koma patsani mphatso yachifundo za mkatimo;ndipo onani zonse ziri zoyera kwa inu. Koma tsoka inu, Afarisi!Cifukwa muperekalimodzi lamagawo khumi la timbeu tonunkhira,ndi timbeu tokometsa cakudya ndi ndiwo zonse, ndipo mumalekaciweruzo ndi chikondi ca Mulungu; mwenzi mutachita izi, ndikusasiya zinazo. Tsoka inu! Afarisi cifukwa mukonda mipandoyaulemu m’masunagongi ndi kulankhulidwa m’misika. Tsoka inuCifukwa muli ngat manda osaoneka, ndipo anthu akuyendayendapamwamba pao sadziwa. Ndipo m’modzi wa cilamulo anayankha,nanena kwa iye, Mphunzitsi, ndikunena izi, mutitonza ifensoLuka 11:37 – 45.Zindikilani tsono kuti sikundi kovuta kusamba m’manja mongamomwe ankafunila afirtisiwo. Kodi kuwonetsa chikondi comwe5

akhristu, ubwino ndi kuleza mtima sikungathe kusuntha moyomlingo umodzi? Cikawapweteka motani? Tiyenera kuwapedzaanthu kumene ali, ndiponso tikhale zonse kwa anthu one.Timachita zimenezi?Mwina simudziwa, Yesu ndi wodzadza ndi cikondi – iye ndiponsoIYE YEKHA ndiye tanthauzo la cikondi cacikhristu, kuleza mtimandi m’mene uli bwino. Zinthu zonse kwa anthu onse? Yesuyekha ndi amene angafotokoze m’mene zinthu zonse zingafikileanthu onse mtanthauzala Atate. Ndipo Yesu adachita zinthuzambili monga kukuwonekam’mwano ndi atsogoleri acipembedzoponkanyoza zocitika pacakudya ca madzulo. Nthawi zina Yesundi akuphunzira ake ankapita munda wa tirigu pa tsiku la sabatandi colinga pamene amutsutsa ankamuwona natanthauzira mwinanaletsa coyambika kalekale ndi Mulungu. Anthu odzikhulupiliramuchilamulowa ankadzika okha pa mtsutso ndi amaulungum’mene iwo ankatanthauzira malemba. Ndipo Yesu analikuwalongosolera zonse bwino bwino osaphatikiza ndi maganizoaumunthu. Chifukwa chiyani? Tikukhulupirira kupeza yankhopamene tipempheraNdikupitiliza ndime imeneyi. Muyeso wazokometsera dzimeneYesu adadzikhazikitsa pamene ankayenda midzinda ndi ophunziraake khumi ndi awiri dziyenera kumachitika ndi muyeso womwewondi otsatira ake lero. Khumi ndi awiriwo,naphunzitsidwa bwinom’mene zikhristu cidaliri ndi amene anali kutsogolera gulu la anthu3108 kuphatikizapo otembenuka oyamba m’moyo wa yesu mkhristupatapita tsiku la pentekositi nadzadzitsa moyo wawo ndi Yesu.Zimene ankabweletsa kwa gulu lalikulu la amene adazipereka kwaYesu ndi muyeso woyenera wadzokometserazo ndi ndondomekozacipembedzo kuti ife anthu tidzigwiritse ntchito mpaka lero.Ndipo cowonadi ciyenera kudziwika kwa anthu mazana mazanaotsonkhana pamodzi a mpingo wakhristu wa m’bayibulo kumenekulibe nkhani yiliyonse yokhuza mapulogilamu, zokometserakapena nthano. Kunalibe comangidwa ndi gulu lililonse, mongamomwe timacitila ife kuti ichi cikutchedwa IBM kapena AMWAYzitalembedwa. Kunalibe kucotsa mavesi ena naikapo maganizoakucenjera kwao. Ndikubwerezenso kunena kuti zowonjezerazathu kumipingo ya Mulungu kawirikawiri zikuoneka ngatimiyambo yopanda ntchito yatsekeleza ciyero, cikhulupiriroceniceni kuti ciwoneke monga momwe Mulungu ankafunilazinthu zikhalire padziko lace zisanakwana zaka cikwi cimodzi(100) atamwalira Yesu.Ngakhale tanthawira kutali kucoka kunjira za yesu, ndondomekondi nthano zathu ndi kudzipweteka zakhala zinthu zimene mibadwoyambiri yapadziko pano ngati zenizeni. Ena atha kutsutsa kutizonse za zipatso zimene zinalipo mwathu zabadwa kucoka kunja,kudzipweteka ndi ndondomeko zathu zoona ndithu. Monga anaamafuna malangizo ndi zipangizo cooneka kuti atengeleko. Anthuolumala amafuna ndodo ndi mipando yoyenda. Kungatani ngatimwana uja atakula? Kungakhalenso bwanji ngati ziwalo zopuwalandi thupi lobvutika linacila? Ndiponso kuli bwanji ngati mpingowokula msinkhu wa Yesu?CHAKUDYA CA MAGANIZO NDI LINGALIROEna mau acipembedzo amene sakupezeka mu Bayibulo, (kutanthauziramolakwika kumaphunzitsa mosamveka kapena mfundo zolakwika.)“Mpingo”, “Utumiki” “Ubatizo”“Cipembedzo” “M’busa, “Pemphero”“Khristu, “Mtumwi” “Cipulumutso”Ngakhale mau amenewa amapezeka paliponse masiku anomcikhristu monga Bayibulo limene timatha kuwerengamcilankhulo cathu limatiwonetsa zoona ndikupemphani kutimuganize amodzi ndi ine mwakamphindi kocepa. Cifukwa ninjimau amene Yesu ananena kwa khwimbi la anthu, ndiponso mauamaene mtumwi Paulo adalembakumipingo tanthawi yimeneyoakutsiyana matanthauzo ndi mau amene timamva ndikuwerengalero? Mwacitsanzo mau oti “gay”, sakutanthauzidwa m’meneankatauzilidwa kale? Akufunana ngati?Ukunena kuti gay mu zaka zapitazo mwavevetsa bwino chipembezochamakon zili ndizotengera zambiri zimene zili zabodza zotengedwakuchoka mu mawu a chipembedzo atathauzidwa molakwika ndikulembedwa munzeru zina, kusiyana ndi Bayibulo.6 7

Zodandauitsa kuti mau amenewa sayimila zimene zonse Yesuali, mwinanso Paulo ngakhaleso ena aliyense amene tingathekumkumbukila. Pamene muwerenga Bayibulo napitiliza yetsetsanikumva zimene anamva koposa kumva m’mene zili mubadwowosatembenuka ndi katanthauzidwe kalero. Thetsani, samalanindichotsekesa ndi chobvuta kupeza coonadi.Ena madziko okhazikika matsiku ano mdziko lonse – amenesakupezeka mpingo wa bayibulo ndi awa: mapempheroakapembezedwe, ulaliki, maphunzilo ala Mulungu, masukuluakolenji achikhristu, makwaya, kuyitanitsa adzilaliki amoto –makaleta ofunsira ntchito, kuyetsa, kuyetsedwa polowa ntchito,kukhazikitsa tsiku la Mulungu ngati tsiku lapadera, kusankhidwakwa anthu kuti adzipempherera msonkhano wa cikhristu. Nthawiisanakwane kulalikira, kapena kutsogolera mayimbidwe ndizina zotere.Kugwira kwa mbiri yakale – Paulo sankanyamulaBayibulo, kulalikira ndi kusukulu za Bayibulo.KUKONZEKERA ULALIKIKumanga Makachisi …………….. Chiyambi ca mizu ya makachisiachikhristu kukuwoneka kuti kuyamba posachedwa mzaka zikwizitatu ndi makumi awiri atamwalira Yesu Khristu (AD) pamenemfumu (Emperor) constantine anawona kuti onse adzipembezozonyenga adali ndi makachisi ndiye nayenso anaganiza kuti Mulunguwake watsopano Yesu Khristu naye adzimangilidwa makachisi.Akaswiri ofufuza zakale sakupeza chotsalira chilichose cimenechikubvomerezana ndi chipembedzo chachikhristu munthawiya Yesu kapena kwa khumi ndi awiri, kapenanso patadutsa zakamazana awiri atapita. Ichi nchachidzikire kuti gulu lokwana zikwikhumi lotembenuka mtima linkapita ena kukachisi wa Mulungu,mwina masunagoge achiyuda ndi makachisi ao, mwinansokumakachisi azipembezo zina. Chikadamveka kwambiri ndiponsochosakanika nthawi yimeneyo kwa akhristu kumanga makachisiakulukulu monga anthu achitira lero nakhala ndi mapempheromomwemo. Koma sanatero mwa nyengo ziwiri, sanatero, cifukwaninji? Chifukwa cilamulo comapita kumakachisi patsiku limodzilopatulika, ndi mwa malo amodzi chitsutsana kwambiri ndi zolingandi zifukwa za Yesu ndi mpingo wam’bayibulo umene adaufera poukhazikitsa. Tengani nthawi zpchepa, pemphelerani maganizoamenewa pamodzi nane amene ali enieni ndithu mwa zimene Yesuanabweletsa kudzakhazikitsa kucoka kumwamba kufika pansi pano- m zimene Yesu anabweletsa kudzakhadzikitsa kucoka kumwambakufika pansi pano – mchiyanjano cha umulungu m’mpingo wace.Chithakukusinthani nthawi yose. Ndipo nchotsangalatsadi,:”Komatu wamwamba mwambayo sakhala m’nyumba zomangidwandi manja monga m’neneri anena. Thambo la kumwamba ndilompando wacifumu wanga. Ndi dziko lapansi copondapo mapazianga. Mudzandimangira nyumba yotani? Ati Ambuye kapena maloampumulo wanga ndi otani? Machitidwe 7:48 – 49”“Ndipo zitseko khumi ndi ziwiri ndizo ngale khumi ndi ziwiri,citseko ciri cose pa cokha ca ngale imodzi. Ndipo kwalala la mzindanilagolidi woyengeka, ngati mandala openyekera, ndipo sindionakacisi momwemo; pakuti Ambuye Mulungu wamphamvu yonse, ndimwanankhosa ndiwo kacisi wace. Cibvumbulutso 21:21-22”Pali mtima wa Mulungu ndipo mpingo uyenera kukhala citsanzocamayendetsedwe ace pansi pano. Mpingo wa moyo, wawo na waokhulupilira nautenga ngati wawo naumangira zipupa nayikakomalata yimene sinkhani kwenikweni pansi pano. Izozo zilibentchito poyelekeza ndi zimene tikulingalira pano. Timangofunakuwona ndithu chikhristu cimene cili ndimawonekedwe achikhristu, koma nayikana ca icho mu umodzi ngakhalenso,payenkha payekha.Kawiri kawiri mau a Mulungu akuchitira umboni wa ulemererowa njira yatsopano. M[ingo watsopano wa ku Aefeso mwacitsanzounkakumana ndi mabvuto oopsya kwambiri. Mzinda umene ujaunacita citsomo ndi zamphamvu za cimodzi za zozizwa za mdzikolonse lapansi kachisi wa mfunu Diana.Kukulirakulira kwa mipingo yotsiyanasiyana mumzinda wao /yimene motsakayika kuti ambiri anatembenukira kwa yesu) analindi kachisi wokongola kwambiri mdziko lapansi lonse. Kodiakhristu adatha kupitiliza bwanji ndi izo? Pauli ankalemba makalataambiri nawongolera maso amitima yao kuti awone masomphenya8 9

a ufumu ndi ndi a mpingo wakacisi nati zimenezi zitha kuwonekandi maso auzimu okhaka. (Yohane 3:3-8, 1 Korinto 2:8-16,mateyu 11:25-27) Ndipo njira yamoyo watsopanoyi yikuposelakwakukulu poyelekeza ndi zimene zimapezeka m`manyumbaomangidwa ndi anthu wamba. Mulungu akukupangilani inumokhalamo m`nyumba ya ulemelero wache. Simungo sangalalandi kamangidwe ka anthu pamene inuyo ndinu miyala yamoyonatengedwakuchoka m`mwala weniweni umene ali yesu mwini.“ndipo anatiukitsa pamodzi natikhazikitsa pamodzi, mzamwambamwa khristu yesu, Aefeso 2:6” pamenepo ndipo simulinso alendondi ogonera , komatu muli amudzi womwewo wa oyera mtima ndiabanja la Mulungu. Omangika pa maziko a atumwi ndi aneneri,pali khristu yesu mwini, mwala wapangodya; mwa iye chimangochonse, cholumikizika pamodzi bwino, chikula, chikhale kachisiwopatulika mwa Ambuye, Aefeso 2:19-21!(Werenganinso: Mateyo 21:1-2; Marko 14:58; Yohane 2:18; 14:1-3-3; 14:15-21, 1 Akorinto 3:9-10; 1petro2:1-12; Yesaya 51:1-2.)IFE NDIFE KACHISI WACE!!! Ndife malo ake! Ndife nyumbayachristu yomangika yimene yiposela zonse, anthu osati malokapena nthawi. Tizakhaladi m’malo, panthawi, m’nthawi zinakoma tikamadzizungulira zimenezo, china chake ndithu citsowekasi mpingo wace, ufumu wace sukufotokozedwa kuti ndi wapamalomwanthawiso yina.Ndipo pamene Afarisi. Anamfunsa iye kuti ufumu wa Mulunguukudza liti, anawayankha, nati Ufumu wa Mulungu sukudza ndimaonekedwe; ndipo sadzanena, taonani uwu, kapena uwo; pakuti,taonani Ufumu wa Mulungu uli mkati mwa inu, Luke 17:20 –21.Ndipo inu musafunefune cimene mudzadya, ndi cimenemudzamwa, ndipo musakaike mtima, pakuti izi zonse amitundu yaanthu yapadziko lapansi amazifunafuna, koma Atate adziwa kutimusowa zimenezi. Komatu tafunafunani Ufumu wace, ndipo iziadzakuonjezerani.Musaopa, kagulu ka nkhosa inu; cifukwa Atate wanu akondakukupatsani Ufumu. Gulitsani zinthu muli nazo nimupatse mphatsozacifundo mudzikonzere matumba andarama amene sakutha,Cuma cosatha m’mwamba kumene mbala siziyandikira, ndiponjenjete siziononga. Pakuti kumene kuli Cuma canu, komwekokudzakhalanso mtima wanu. Luka 12: 29 – 34.”Yesu ananena naye, Tamvera ine, mkazi iwe kuti ikudzanthawi imene simudzalambira Atate kapena mphiri ili kapenam’Yerusalemu. Inu mulambira cimene simucudziwa ife tilambiracimene ticidziwa pakuti cipulumutso cicokera kwa Ayuda.Koma ikudza nthawi, ndipo tsopano iripo, imene olambira oonaadzalambira Atate mumzimu ndi m’coonadi pakuti Atate afunaotere akhale olambira ace; Mulungu ndiye Mzimu ndipo omlambiraiye ayenera kumlambira mumzimu ndi mcoonadi Yohane 4:21-24.Koma tsopano podziwa Mulungu inu, koma makamakapodziwikandi Mulungu, mubwereranso bwanji kutsata miyambo yofoka ndi yaumphawi imene mufuna kubwerezanso kuicitira ukapolo? Musungamasiku, ndi miyezi ndi nyengo, ndi zaka, ndiopera inu kuti kapenandadzibvutitsa ndi inu cabe (Agalatiya 4:9 –11!)Ndicamtengo wace ndicotsangalatsa kuwona zimene Mulunguwatichitira ife ndiponso mwa ife nakhala mwacizalo. Kukhazikikamukukonzeratu malo ndi nthawi ndiponso mfuupa za anthu,m’malo momulola mutu wa Eklesia Yesu mwini kutsogoleramiyoyo ndi misonkhano yathu ndikusemphane ndi ulemerero wamulungu wacolowa. Panopa tikumaganiza kudziteteza tokha ndimapembezedwe abwino, titakonzelatu mocenjera malankhulidwe(nkutheka kuti akucoka mbayibulo) nakhazikitsa matsiku,masabata, ngakhalenso zaka ndi nyimbo zonse kuphatikizapo cinaciliconse cofunika mapemphero patsikulo.Sicinali cikonzero ca Mulungu kukhala ndi cikhristu cimenecikudziwika ndi maganizo a anthu, ndondomeko pasabata nakhalandi anthu obvala bwino, nawauza bweretsani mzanu patsabata,nakhala ndi gulu lotchedwa komitiyi, akatakwe amene alembedwantchito ndi mpingo kukhala mtsogoleri wawo zinthu ngatizimenezo. Kuyambira kale tawona zotsatira za zinthuzi zimenezilikutali kwenikweni kuchoka kunjira ya Yesu Khristu, ndi khumindi awiri ngakhalenso mpingo umene udawadziwa.Miyoyo amuna ndi adzimayi, atsikana ndi anyamata yakhalayosabvuta kupezeka m’masewero apansi pano ngakhalensokugwiritsidwa ntchito ndi satana. Zoonadi ali pamabvuto. Koma10 11

mpingo weniweni ndi umene Yesu Khristu adaunena kuti makomoadziko la akufa sadzaulaka uwo. Ndondomeko ndi miyambozalephera. Yekha Yesu alimkutchulidwa mwa anthu ace – mpingoumene m’coonadi walumikizana naphatikizana pamodzi nalandiracithandizo la Ufumu wa ansembe, banja logwirira ntchito mnjira yace,osati munthu amene sangathe kucotsa mphamvu zakumdima.Tikayang’anitsitsa kumbuyo timapeza mbiri za cipembedzonawona m’mene tinafikila pamene tilikupeza kuti kacisiwomangidwa zinayamba kukhala mbali yacikhristu mzaka zanalimodzi ndi zikwi zisanu zambirimbiri. Gulu limene linkasusanandi mau a Mulungu (protestants) linapitiliza kugwiritsa ntchitomakacisi aciroma itantha nthawi yakukonzanso ndi mtumikiwotchedwa Martin Luther, ndipo anayamba kudzindikilitsa okhanga nawonso ndi aciroma. Monga timamvera mtumwi Paulo ndicimodzimodzi lero. Kwina kusinthika kofunika kwambiri kunalikuwonjezekeredwa nthawi ya Luther. Izi nzotsacita kufunsandipo tiyenera kutsangalala kuti munthu monga Martin Lutherankafuna kutaya moyo wace polimbana ndi zipembedzo zophukamnsanje naphatikizana ndi nyumba za manja a anthu anthawiyokomabe muyeso wakanidzilidwe kakakulu kamene kakutsogolerazipembedzo zambiri mpaka pano kanatengedwa pamodzi kucokam’masiku a Luther ngati cinthu copembedzedwa.Mpingo umene Yesu anaumanga (ndipo akuumangabe) siuli pano, kapena apo. Panthawi, sukugwirizana ndi malo amfumu monga momwe zipembedzo zones za padziko lonse ndizaciyunda zinkacitira.Kodi zimenezo zikutanthauza kucepa kwacocitika, cipatsongakhalenso mwina kucepa kwa msonkhano mumpingo? Iyayi,makamaka Mulungu adalora kusokonezeka kwa chipembedzochake ndikukweza zoyamba zace ndimaganizo a anthu chifukwachakulimba kwa mitima yao. Koma sidzinali choncho paciyambi;Mulungu anawapatsa ana ace loweluka tsiku loyera. Anatipatsa ifeYesu kukhala sabata yopumila (Ahebri 4:1 – 11; Mateyo 11:25 –30)Tsiku lililonse kaya patokha kaya pamene titsonkhana pamodzi,nkofunikilathu ngati tikhaladi ndi Khristu m’malo a ufumunakhala ndikukhala nazo zonse mwa iye. Ngati tikhaladi mwa iyekusokonezeka ndi cikhalidwe, kupandilathu masiku ndi nthawi ndimfundo zongopeka zimatchinga poyelekeza ndi zimene zikanacitikakopanda zimenezo pakati unsembe wacifumu. Anthu a Mulungundi odzindikira pamene anamasulidwa kukhala moyo wacepamodzi kusiyana ndikungowelenga mawuwo ndikungowayimba.Kukada khala choncho m’badwo wosatembenuka ndi wosadziperekawa amuna ndi azimayi ndi umene ukadakhala ukufuna ufumuwao ndi nthawi ndi malo, pakalendara ndi dongosolo ladzimene zizachitike pamene tizafika kumwamba.cifukwa ninjiakanayika kufuna kwao mdzkometsela ndi zikhalidwe kapenansocikonzekero. Cifukwa kufuna ufumu wa Mulungu ndi canthawiyose, zowona kutsatira moyo wa Mulungu ndikusonkhana cifukwaca iye kawirikawiri poyela ngakhalenso kupita nyumba ndi nyumbasikoyenera ndithu kusunga chilichonse cha mzaka makumi awirimakezana mnthawi ya mafano.Iyitu ndi njira ya Mulungu, dziko loyela nafuna chiyamba ufumuwake, ndi Yesu akukhala mkati mwao:Ndipo anali cikhalire mciphunzitso ca atumwi ndi m chiyanjano,m’kunyema mukate ndi mapemphero, koma panadza mantha paanthu onse, ndipo zozizwa ndi zindikilo zambiri zinacitika ndiatumwi.. Ndipo zimene anali nazo ndi Cuma cao, anazigulitsa,nazigawira kwa onse, monga, momwe yense anasowera. Ndipo tsikundi tsiku anali cikhalire ndi mtima umodzi mkacisi, ndipo ananyemamkate kunyumba kwao, nalandira cakudya ndi msangalalo, ndimtima woona. Nalemekeza Mulungu ndi kukhala naco cisomo ndianthu onse. Ndipo Ambuye anawonjezera tsiku ndi tsiku ameneakuti apulumutsidwa. Machitidwe Atumwi 2:4 2 – 47”Chikhalidwe chapa ndime yapamwambayi cimacitika ndi anthuosatembenuka, akunja okhalamo, alendo amene anatembenukakucoka ku umbombo kulowa mu ufumu wa mwana wacewokondeka zoona ndi zosabvuta kwa anthu amene ali Yesu mwininakhala mkati mwao, amayenda monga iye anayendela, nazazandi changu ca mnyumba ya Atate. Mukangacotsa Luka 6:1, 14:35ndipo muzatsilidzira ndikanthu kena monga Machitidwe 2, Kodimungaganize zifukwa zina zabwino zimene zingakuletseni kukhaliraiye amene anakuferani inu? Ine palibe, tose pamodzi tilibe.12 13

MBIRI ZINA ZOTSANGALATSAPanopa timamva citsoni kukhala ndi mpingo wopanda maphunziroaza Mulungu (Sunday school) ena akunena kuti akazakula ndipamene adzakhala ndi mpingo weniweni wofanana ngati umenePetro ndi Yohane ankautsogolera umene unali ndi maphunziroala Mulungu angopangidwa posachedwapa ndi anthu nakulitsadzimene Yesu ndi atumwi nazicotsa m’makalasi zitakhazikikapakati pa ayuda ndi agiliki.Tawonani izi: zokhomakhoma zinakhazikika mnthawi yakusadziwa Mulungu Kalekale ndi AromaGuwa – Zinakhazikika atamwalira Yesu (AD) mzaka zikwizisanu ndi chimodzi ndi Aroma nthawi ya (1520 AD) mnthawiMartin Luther.Zowaza mkapu - mnthawi ya 800 AD.Maphunziro azitsogoleri (seminaries) - 1300 ADKuphunzitsa anthu (atsogoleri) ndi cacilendo kwambiripowona macitidwe ndi maphunziro a Yesu ndiponso cipanganocatsopano. Mu ufumu wa Yesu anthu ankakula mmoyo wakuyaosati mocita kuwapopa ngati tchubu kapena tili kuwaphunzitsiramakalasi utsogoleri.Makolenji acikhristu - anayamba nthawi ya 1640 AD kuperekamaphunziro acikhristu.Kubvala kwa tsiku lasabata – Nthawi yakusadziwa (Dark ages).Matayi apakhosi - anayamba ndi anthu pofuna kupikisana kuwonaamene wabvala capamwamba kwambiri pacakudya camadzulo.Zobvala zazitendene zazitali - Zinayamba kunena kuti ameneamafufuza zamakezana ndi ena oyesa dziko kucoka ku Iguputosankafuna kupanda zosala zatsiyidwa! Dziwani kuti palibecolakwika ndi izi wazokha monga malaya abwino, tayi wapakhosingakhale zitendene. Koma kudalira zobvala zokongola patsikulasabata m’mamawa, mndimvetse kuti zimatsutsana ndi ciphunzitsondi moyo wa yemwe ali mutu wa mpingo Yesu Khristu. Cabwinongati munabvala bwino popita kumaliro am’bale wanu, mulekelenjikubvsls cimodzimodzi popita kutchalichi?Ngakhale cikamveka coyenera kale mnthawi ya 20 th Century,m’mayiko monga America ndI Ulaya sidzinali m’mene Yesuankafunila kapena kuti mpingo unatero kuti anthu azibvala chonchokupita kutchalichi. Yesu sanacitepo, ndiponso nafe sikofunika.Ndikudziwa kuti zonse izi zabveka zacilendo kwambiri kwa omweanakulira muziphunzitso osati za Khristu. Kumbukilani kutisitikuwonananso zotsatira za mpingo tikuwuwelenga m’bayibulotikuwonanso ngati? Ichi sicinthu cocepetsedwa. Tinawongedwa ndicikhalidwe ca anthu ndipo panopa nthawi yakwana yoti tiyikile njiraza chibwanazi kumbuyo, (Marko 7:13, 12:38 – 40) Monga MtumwiPaulo analemba kuti tisaweruzidwe ndi wina aliyense pamene mulinkukhala mu ufulu wa uthenga wa Yesu (ndipo tisatsiyane ndithukoma tiwone zinthu m’njira imene Mulungu amayiwonela.Apatso Pali Zina Zodabwitsa - Tikanena za Alaliki, Abusa(mlaliki wamphamvu, wotsogelara zocitika mwina titi (Masterof Ceremony MC) ngakhalenso atsogoleri apa mpingo, zimenezizinayamba mnthawi ya 1520 AD. Martin Luther ankagwiritsantchito ansembe akale, ongotembenuka kupitiliza kuika maliro,kuyendetsa kapena titi kumangitsa maukwati, ndipo mnthawiyace ya utsogoleri wace anthuwo a mkayendetsa zonse zapatsikula Mulungu, kupereka mau, kapena ulaliki. Mukuwona kufananakwace kwa zanga, zanga.Tiwonetso za makola oyela apadela obvala mkhosi atsogoleri– indedi Yesu anadzudzula cizolowezi comabvala zinthu zapadelandi colinga cakumukopa wina mu cipembedzo cake kapenakudziyeneretsa, tiyeni tibwelelele nthawi yamasiku amenewa.Posachedwapa ena akunena kuti tili ndi mangawa ndi mpingo wamethodist cifukwa coyambitsa zimenezi mnthawi ya ulaliki wao.Makamaka pamene ankayenda kucoka ku malo ena kupita kwinanayenda pa akavalo, nafikanso pomatha kubvala zotseka kukamwandi mfuno zao. Ankamasulira pansi malamba agho kuchoka mumakosi agho atamaliza kulalikira.14 15

Mnthawi ndi pamene kumkabadwa cisumo comabvala makolalaautsogoleri zacabecabe siconcho kodi?Tibwele pa nkhani yamapini, mabelo, maguwa, cigulu coyimilautumiki, dongosolo la ngati zimenezo, ngakhalenso izi “JoeSchmoe Ministries, Inc Tipitilize za zimenezi zinkawonetsacikhristu mnthawi yimeneyi zoona anayika zatchinga mnjirakutitsekeleza kuti tidzadziwe za moyo wa okhulupilira oyambanga ansembe a cifumu ndi kufuna kunena mobwelezabwelezamfundo yimene ena atha kukuwa kunena Allelluah natulutsamau amene sanalikudziwika kuti ali mkamwa mwao, kuyankhulandikupanganso ena zinkhonono nalephera kupuma atayambitsanthenda ya mtima.Ambiri amene amadzitcha okha akhristu lero alandidwa ndiamene amawatenga nakhadzikika mcisoceletso caciroma nadziwapang’ono kwambiri mawu am’bayibulo ndi m’mene angakhalireolandilidwa nacitira pamodzi ndondomeko nawayika muutsogoleri wamipando yazipembedzo. Ngati mlengi wazonsezokhazikikazi ankapezeka m’magulu athu, sicikanathandiza, komakukhala kutali kwenikweni kuposela apa. Eni a mpingowa amenetawatchula pamwambapo antha kuwoneka ngati ndi abwino,poyetsetsetsa njira yowonetsera mipingo yao kuti sidzingayendekopanda m’modzi wa iwo. Ukaganizira zimenezo kuti ndi m’meneukupeza kodi nkuganiza ngati ndi m’modzi mpingo wa mphamvuwa m’buku lamacitidwe (pakuti iwo sanali concho) kapenaukuwona kusapha tikidzidwa kwakulu? Kodi ngati titacotsa ameneakudzitenga ngati ndi eni ainu kodi pangatsale munthu mumpingowanu? Ngati mpingo wanu sunakhazikike ndi kuwonjezapo umodzindi mphamvu ya Mulungu koma umangokhazikika pa zofunaza eni, kukonza kayendetsedwe, kumanga, kuyimitsa azitumikiamphamvu, Gulu loyendetsa Gulu loyendetsa mpingo, ndikukonza zokumana kumana kawirikawiri ndiye kuti mwamangapa polakwika. Pamene kayendetsedwe aka ndi zophatukiza zacendi kapangidwe ndi cilendo kumpingo wa m’bayibulo (ngakhalempingo utakula mpaka anthu 15000 kuwonjezerapo mamembalaena am’mpingo momwemo) ici ndi cilamulo cokomatsela akhristuamunthawi zamakezana (20 th Century) abale sidziyenera kutero.Kunena zoona zonse zimene tikangamilakozi ndi zofunika kambakoti tikutsoweka ubale ndi Mulungu weniweni wa zonse. Zimeneiye ankafuna inu mucicite m’mpingo wace, Ahebri 8:1; 10:25,Akolose 2:16 – 17).Ngati timuziwa iye mcoonadi, citetezo cathu canthawi ndinthawi citsogozedwa mwa ubale osati mwa cilamulo. Zoyambazamaciridwe a mphamvu ya Uzimu m’mipingo umene tikuwutchulam’buku la Machitidwe mutu 1:1 m’mene tipeza zoti Theo – philus– kutanthauza okoma Mulungu osati Theo – Logians, amaphunziroa pamwamba. Mbiri ya macitidwe aulemelero pakati pa anthuwamba sizinalembedwa kwa anthu odzikweza pamaso a Mulungu.Pafunika kuganizira kwambiri pamenepo, kuti umasukilethumoona mwa Yesu. Mucikhristu canu, muyenera kukhala ndiubale mwacikondi osati mwacilamulo. Ndikhulupilira kutizonsezi zikutitengela ife sono kukonzanso siconcho? Zimenezisidzikuthandauza kuti sono tiyamba kuphunzira ciphunzitsozacilendo copanda zokometsera (ngakhale zokometsera ziyenerakuwonongeka moti tiphunzire kudlira Mulungu, nacita zonse pansipa utsogoleri watsopano wa Ambuye wa mpingo? Makamakatisowekadi kucilitsidwa kusoyamba zamakezana (20 th century)zamafano nadalira nyumba sokumanamo, kayendetsedwe kaanthu, madipuloma, ulesi mawayilesi akanema, zitsangalarozopanda pace kapena zaucimo za matupi athu, nathamangirazotengeza, nathamangira zotonthoza, ndi mafano osiyanasiyanatosawoneka miyoyo yathu. Pamenepa tithakusiyanitsa pakati pampingo ndi dziko osati mthupi, pamene mafano aswekela pansiamene atitchunga ife kucoonadi (Ezekiel 14:3).Ndipo tidzatha kutsangalala ndi Yesu nakhala ni moyo watunthuwa ulemerero umene anauyang’anila natisiyila ife, Ahebri 3:1; 12:1-2; Yohane 17:5, 22, Luka 12:32; Mateyo 16:19, 13:43; 13:52.Siyanitsani mau amenewa ndi zimene Yesu anasiyila ameneadzayenda m’mawonekedwe osati mwa iye. Mateyu21:43; 23:13;23:38; sibwino nditsilize ndi ndime yazolemba zina. Izi nzafupindipo nzothandiza makamaka popitiliza mapephero ndi kuganizira.Kumbukila kuti pamene mudzilandira kopanda maganizo atsopanocitsiliziro chake cikhala coyipa kuposa coyamba. Pokhapokhatidzichotsa mukukula kwathu ndi pamene tidzabvala za umwana waMulungu nadzindikila cifuniro cake. Tikangotembelera ndi kucotsa16 17

cobvala ca umwana tidzakhala ndi mwana wamaliseche, wobvutika.Munthu wolumala akusoweka comuthandiza kuyenda (wheel chair)nyala zakunjinga yoyendapo, malo apadera wosungako, ndi maloake ake osambako. Kungakhale bwino bwanji kucilitsa munthuameneyu malo momukonzera zinthu zomuthandiza zapamwambamomputsitsa (ndondomeko, nthano, zolinga zopanda pace)Mose anatumikila molakwitsa, m’malo ndi zinthu, ndi nthawi, ndizopanga cifukwa cakuuma mitima yathu, koma kuyambila paciyambiisinali concho. Tiyeni tisinthe tithetse zimenezo. Tipilize.PALI CIYEMBEKEZOKodi ufumu wamulungu ukuwoneka bwanji? Kodi mpingo uneneukuyenda pamodzi ndi Mulungu ndi mcisomo conse ukuwonekabwanji? Kodi ngingazindikile bwanji Mzimu wa khristu ndi njirayake yabwino ya anthu ace ndi ine ndemwe?Yesu mkwati, mpingo wace. Ali mkazi wamtengo wacewapamwamba mkazi wokonzekera kubweranso kwa mkwati,Mfumu ya ulemerero, ali mkazi wa mpingo wa ulemerero, wopandabanga, kapena makwinya, ngakhalenso kacilema kena kalikonse.Mkwatiyu ndi gori lofanana ndi Yesu – wacifundo, koma nazazandi ukali kwa cinyengo, wotsamalitsa natsatira ntchito ya Atate acemosabwezako. Uyu ndi mpingo umene Yesu anaugula ndi mwaziwa iye mwini.Uzakhala mpingo umene siukumangidwa ndi nthawi kapena malo,koma nthawi yose paliponse poyela nayendanso kupita nyumbandi nyumba. Udzakhala pamodzi naphatikizana ndi thandizolathupi lace, nakhalidwe wina ndi mnzake, navomelezana macimowina ndi mzace, nalimbisana wina ndi mzace nthawi zonse ndipopopanda wina wolimba mtima kamba kacinyengo caucimo,nthawizonse nakondana, natumikilana, nasenzelana zowawa wina ndimzace mwa cimwemwe ndi ciyamiko. Nakhalanso ndikucepa kwamisozi. Kupezeka kwace kuzaphatikizana ndi kasonkhanidwekamizinda ndi m’manyumba kwa anthu ake onse. Ndipo unyinjiwa iwo akukhulupirira anali wamtima umodzi kuti kanthu kacumaanali naco ndi kace ka iye yekha.Mpingo uzazindikilidwa ndi mphamvu yace ndi cisomo cace.Tchimo lizawonekera ndi kucotsedwa ndi mphamvu ya ulemererowace wosatha m’miyoyo anthu ali mumpingomo. Amusingaazamasulidwa, kuyimbira nyimbo za Mulungu sikudzakhalakwa colemba mbuku nthawi isanakwane koma kudzakhalakwa kutsika kwa zimene Mulungu akucita nthawi imeneyopakati pa anthu. Yang’anilani amene azazidwa ndi cimwemwe,cikhulupiriro, oyera mtima ace atha kuzaza ndi nyimbo penapaliponse ngakhale pamene mpingo uli m’nyumba yodyela.Cimene cili ceniceni pamalo amodzi ciyenera kukhala cenicenipaliponse. Vinyo ndi madzi a moyo ali ndi tanthauzo latsopanomwakudziwa izi. Ndiza m’bayibulo, zabwino bwino nazaza ndicikhristu ca Yesu.Tonse ndi ubale weniweni tizakhala monga Ambuye anacitira.Yesu mkhristu wa Mulungu tsono akhala mwa ife payekha payekhangati anthu ace, Akolose 1; 26- 27; 3:4; Gal 2:20; Macitidwe 17: 28;Aefeso 5:18; 1 Yohane 2:6; Aroma 8:9.Ndime imeneyi ndi citsanzo cosatha campingo umene Yesuanaukhazikitsa, ndipo cilica m’badwo uliwonse umene udzayendandi iye, mwa mzmu wace.Mzimu wa Ambuye Yehova uli pa ine, pakuti Yehova wandidzodzaine ndilalikire mau abwino kwa ofatsa, iye wanditumiza ndikamngeosweka mtima, ndikalalikira kwa amusinga amasulidwe, ndi kwaomangidwa kutsegulidwa kwa m’ndende, ndikasikire caka cokomeraYehova, ndi tsiku lakubwezera la Mulungu wathu. Ndikatonthozemtima wa onse amene akulira maliro, ndikakonzere iwo ameneakulira maliro mziyoni ndi kupatsa cobvala kokometsa m’malomwa phulusa, mafuta akukondwa m’malo mwa maliro, cobvalaca matamando m’malo mwa mzimu wopsinjika kuti iwo achedwemitengo ya cilungamo yakuloka Yehova, kuti iye alemekezeke.Ndipo iwo adzamanga mabwinja amibadwo yambiri, ndipo alendoadzaimilira ndi kudyetsa magulu ako, ndi anthu akunja adzakhalaolima ako ndi kukukonzera minda ya mphesa,Koma inu mudzachedwa ansembe a Yehova, anthu adzoyesaniinu atumiki a Mulungu wathu; inu mudzadya Cuma ca amitundum’mudzalowa mu ulemerero wao ( Yesaya 61:1-7; Luka 4:18 – 19).18 19

Panopa tinene kuti zonena za Mulungu nzabwino koposa tsikulamunthu, siconcho kodi? Ndipo mipingo yotereyi yilipoyimene matsatira zonena za Mulungu. Ngati ufuna ukalowendikutsimikidzileni kuti kudzela mudzowawa zambiri tikalowemu ufumu wa Mulungu. Mutha mudzonsezi monga winaaliyense akucitira?Mungathe kulipa mtengo wace koculuka koposa m’menetingapemphere kapena kuganizira, mwa mphamvu ya iye ameneagwira ntchito mwa ife, kwa iye yekha kukhale ulemerero mpingo,kunzera mwa Yesu Khristu kupitilira mzaka nzonse, dziko lonsekosatha, Ameni; Aefeso 3:20 Amen.MAU OMALIZACakhala ciyembekezo ca mtima wosweka uliwonse, munthuwokonda Mulungu mwamuna ndi mkazi kuti mwina ulalikiwina wabwino, wina watsopano ndi kuwonjezekela mphamvu,ndondomeko, kacisi womangidwa watsopano ungathe kucilitsazilonda ndi zikhumudwitso za mipingo yao. Mowona, ophumziraa Yesu, owopa Mulungu ndi wothedwa mphamvu, cifukwacakusathandizidwa nawona kutha kwa mabank kukukulirakuliramipingo yao muwelengela anthu apadziko osayanganila zimeneMulungu akuletsa. Akuyanganila moopsya muja, kuti ana oposa60% alinkulowa banja nthawi isanakwane mochepa zaka khumi ndizisanu. Ngakhale pali citsimikizo cosakhazikika, kuyi mpingo yaophunzirayi ndi mabungwe ena, sakukhala mucizalo cha mphamvundi chikondi ndi ciyero ca Mulungu wathu, ena molekelera ndimwacifundo nazitchinga okha. Cifukwa zokakamila kuzikhalidweza anthu, zimakhala mantha akukanidwa, mantha akulephera,mantha akucotsedwa ntchito yao ya utsogoleri. Nalekerelazokometsetsa zao ndi ziphatikizo cifukwa cakudzikonda ngakhalecolowa ca m’banja. Yanganilani zifukwa zobisikadi mwa iwoamene akwiyitsidwa ndi maganizo ena apelekedwe apo. Pamenemuphulitsa chubu wakunyengelera ndi muzu wacipembedzokotheka kukumana ndi musutso umenewu monga Ambuye Yesuadakumanilana nazo. Khala okonzekera izo, nawayamba ndinzeru ndi cikondi. Koma matsiku oyelekeza anapita.Tiyenera kupitila pamodzi patsogolo ndi Mulungu wathumnzaonse iye watikonzera ife. Mneneri Yesaya adanena kutimau a Mulungu sazabwerela chabe. Yesu analongosola mopitilizandi kulamulira mwa mphamvu. Ambuye wathu anatiphunzitsakuti pali cinthu cimodzi cimene cithetse ndi kuwononga mau aMulungu m’miyoyo yathu.Muyese cabe mau a Mulungu mwa mwambo wanu umenemunapereka ndi zinthu zotere zambiri mucita. Marko 7:13.Pomaliza…20 21

koma okondedwa takopeka mtima kuti za inu ziri zoposa ndizophatikana cipulumutso, tingakhale titero pakulankhura, pakutiMulungu Sali wosalungama kuti adzaiwale ntchito yanu, ndicikondico mudacionetsera kudzina lace, umo mudatumikiraoyera mtima ndi kuwatumikirabe, koma tikhumba kuti yense wainu aonetsere cangu comweci colinga ku ciyembekezo cokwanilakufikira citsiriziro, kuti musakhale aulesi, koma akuwatsanza iwoamene alikulowa malonjezano mwa cikhulupiriro ndi kuleza mtimaAhebri 6:9 – 12”DZIKO LOPANDA MIZINDA(Fanizo)Ganizirani kwa kaphindi kamodzi mizinda kulibe amene payenkhaazatha kudzindikira kapena kunena kuti mzinda ndiwantchitoyanji. Moyo wakhala wa mizinda, mwa cigulu ndi m’maphunziro,m’badwo uno, mbiri yikunena kuti mizinda yinali ya amunaamene akadzitcha okha amunadi, ndipo anthu ndi mabanja analiciculukire koposa malo okhalamo.Imani, ndipo ganizirani ndi ine mwakamphindi kuti kungakhalebwanji kukhala m’dziko lapansi pano popanda mizinda.Tangonjetserani kuti gulu la anthu m’badwo umene uja waganizazosintha zinthu ndikuzipanga m’mene ziyenera kukhalira.Ataganiza kubwezelanso mizinda, nakhadzikitsa mizinda ngatimalo ogwirirako zonse pamoyo wao. Ikanatchedwa mizindawaliyense kungokhala mizinda wogwiritsira ntchito. Coyambakucita cikanakhala, mwacilengedwe kupita kunena akusungilakomabuku kapena malamulo kuwerenga, kuwerenga, kuphunzirachilichose ca mzinda.Pokhazikika mukufufuza kwao, anagwirizana pamodzi kutiadzabwezeletsa moyo wamizinda mibadwo wao. Pamodziakamanga nasuntha mizinda ndi matabwa, namalizira ndi maloamalonda, odyelamo, mahotelo, nyumba, mabanki, masukulu,misika, ngakhalenso kokhala acitetezo (police station).Anthu adziperekawa amuna ndi akazi anantha ntchito yobweletsasomzinda weniweni ndi moyo wace kudziko losowa lopanda mizinda.Anagwirizana kuti mwa ora limodzi tsiku lililonse adziphunziramoyo wamizinda. Munthu amene ankasewera masewero enangakhale sanal wacitauni weniweni anayamba kuzala timasambakukayika mkasitolo kake. Wogwirira ntchito yopereka ndalamam’banki ndi amayi ace ndi adadi ace nthawi yonse ankaganiza kutiiye azakhala ndi ndalama zambiri masiku ena anapeza timadolatocepa kutsogolera gulu nafunafuna kutero anapeza mabuku ocepakuti akapatsa ana ake ndi kugwiritsa ntchito kusukulu.Ndipo wapolisi amene ankasamalira ofesi yace kudzera m’mabukuanapeza mabvuto cifukwa mabwana ake kawiri kawiri ankacotsamabukuwa mukabatiyo. Monga tauni mfuti sidzinakhalekonso,cimenecho chinali cosabvuta. Kumene kunali zocepa mu nthawiya makezana mzaka za makumi awriri ndi mphambu ziwiri,zosakhazikika konse.Napanga kafukufuku mucilankhulidwe ndikupeza njira popandanjira. Nasunga buku limene linali ndi mfumbi limene linali ndinkhani yoti kumangalande mzaka za muma 1980 apolisi adziwikakuti (Bobbies) sankagwiritsira mfuti, m’malo mwace ankagwiritsirazophulitsa utsi. Ndipo mukamvekedwe kace cina bwino kwa iyekuti wa polisi akufunika mfuti yokha mnthawi zoyambilira pameneankazikhadzikitsa monga anthu adindo. Patapita izo anaganizakuganiza, kuti anthu apita patsogolo, concho sikunali kofunikansomfuti kutsimikiza maudindo aakulu akulu. Mzaka zina zamuma1980 anthu ankagwiritsilabe mfuti zinali zacizolowezi ngakhale zinalizamakezana ndiponso zimaonetsa kutsazindikira muzimenezi. Ndiponthenda yimeneyi mathedwa. Mfuti sinali yosayenera mcikhalidwecao. Sidzimamulola kucita ntchito m’mene yiyenera kukhalira.Monga mbali yopindula anayamba kupangitsa maphunzirondi misonkhano ndi apolisi, kamba koti maphunziro onseazoyamba zao.Mwaconcho anthu ambiri amayi ndi abambo okhulupirika ankapitatsiku lililonse, mwacipembedzo kuzinyumba zao zamatabwakukaphunzira moyo wacitauni. Monga anthu amutauni anagulazakudimba, masamba ndipo mwini dimba nathamangila ku bankindi ndalama zimene anazipeza mzogulitsa. Ndipo wapolisianayimilira namuteteza mwini munda uja kuti acifwambaangamulande Cuma.22 23

Mphunzitsi wamkulu analikukangalika naphunzitsa. Ndipomwa ora limodzi tauni imeneyo inkakhala ndi zokambilana tsikulililonse ndipo aliyense anayetsetsa (kamba ka zolinga) kugwiritsakayankhulidwe ka makezana kam’matauni masikuwo. Conchontchito zao za m’matauni zinali kuwakwanila.Iyi yinabvomerezedwa kuti inali nthawi yoziwika ya chete kwaanthu a ambirimbiri. Indedi nthawi zina kunkawoneka mabvutopoti dzimenezi ndizoyembekezereka. Ena atha kunena kuti zonsezatsopano ndi zapamwamba zomangidwa m’matauni zimenezinkakulirakulira zinacoka kumagawamo kapena kudziwonetsa.Ambiri anamva bwino kwambiri ndi maganizo wotsatira cowonadi,kukula ndi kumadzalanso m’mataunimo.Tsiku lina munthu wina wakale wocokera mtauni yeniyenianabwera. Anawona pamene anthu m’tauni ya mwiniyiankayendetsera malonda awo. Ankathamanga apo ndi apa ngatikuti zotsatira zamalondawo zinali kudalira iwowo. Pamwambapazonse nkhaniyi yakubwezeletsa moyo wamutauni ndi yofunikadikwambiri. Mkulu wocoka kumudzi wakaleyo adasweka mtimanatsokonezeka, nazizwa, ndipo nakwiyitsa onse nthawi yomweyo.Kodi zonsezi zinali za nthcito yanji? Atikubwezeletsa moyowamutauni – zimenezi?Anadela nkhawa kwambiri ndi kusangalala kuwaphunzitsa iwoamene analikuwonetsa kwambiri moyo wamutauni koposa zimodzindi za mtauni. Mabuku onse ophunzira anali nawo mnthawi yaoanawathandiza kucotsa cymene cinkawoneka cokwanira moyouliwonse wam’tauni, kaciduswa pakaciduswa koma kopanda moyouliwonse kumbuyo kwao.Mkulu wongobwelayo ankabvutika kwambiri kufafana ndi miyoyoya anthu amutauni. Koma zimenezi zinali bwino bwino. Anthungati banja ili. Zoonadi, pali mabvuto koma sankacotsedwazisawawa, m’malo mwace ankadzikweza kukhala oyera kuposainu. Ananena monong’oneza kwa wina ndimnzake pameneankadutsa m’mizinda. Tikudziwa zoona kuti ife tili amutauni.Anali ndizibvomelezo ciliconse ankacifuna.Pali colikwika kodi kukhala ndi ndalama ku banki?Kodi simuli mabuku okwanila musukulu?Pamene ankawonetsetsa zotsatira za mkulu wacilendo ujandi mabvuto ace pamene sankatonthozedwa mafunso awoankakulirakulira.Yetsani kutenga ndalama ku banki muwona ngati gulu la apolisisilikugwira ntchito anakuwa.Mvetsera ngati sufuna m’mene tikumangira apamu tangoyambanyumba yako pano wekha. Takoleza moto wowotha ngatiukufuna. Ukudziwa kumene malo osangulilako zinthu ali. M’malomongonenanenana kwambiri bwanji osamamanga limodzi ndi ife?Kodi iwe ubwino kwambiri koposa wina aliyense?Nkosafuna kunena kuti mkulu wacilendo ufa anacokamodzidzimutsidwa ndi kukhumuditsidwa. Ndipo anthu amutauniankapitabe mokhulupilika mutauni tsiku lililonse panthawiyoyenera pena paliponse mpata unkapezeka ndipo pamenemakomo ankatseguka khala okhulupilika mpaka imfa.Modzilemekeza ndi mwadongosolo mukuwona moyo wamanthandi kudzikudza, simawalore iwo kuti atsiyanitse pakati pakupitakutauni ndi kukhala wa mtaunimo.Tikupempha kuti anthu mutauni atiphunzitse kuti tisasokonezeceniceni ndi kadziwidwe ka kalekale. Tikupempha kuti tikhazikikepang’ono koposa m’mene kumakhalira, mkati ndi kunja ndi kutitisangowonjezera ubwino wa muyeso wa sikelo kapangidwe.Maphunziro awasukulu akusunga ntchito ya eni ace.Sidzikupangidwa osati ndi tauni kapena mpingo. Ndiponso kunenaza matauni kapena kuwerenga za mtauni sikungafanizidwe ndicidziwitso ndi cimwemwe ndi phindu lace la moyo wamutauni.Ngakhalenso moyo mu ufumu wa Mulungu. Phindu ndi mphamvuya moyo wamutauni sidzidzakhalako pamene matauni, ndi mipingoyikhalira yapamwamba muzochitika za eni ake. Musakhutirekuyenda m’malo osungilamo uchi. Lowani mcimeneci ndi moyowamtima wonse. Khazikika osati cifukwa cilamulo cinaciliconse,kapena kukhala ofatsa mzaka zoonjezera khumi kapena kupyola.24 25

Mayankhulidwe amphamvu mutayima kumbuyo kwa guwakusacotse coonadi ca Mulungu, cocoka mtima wace pa anthu ace,masiku ano. (Aefeso 3:10) Ambuye atidalitse nchikutithandizapamene tonse tifunafuna kukhala anthu ace, mkwati amenewadzikonsekera kubwelanso kwa mkwatibwi, “ Ufumu yaulemerero Ambuye, Yesu Khristu. Dzina lace lilemekezedwe.26

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!