17.06.2013 Views

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

Mmene Mungawerengele Tchati cha

Moyo wa Mwana

Mizere iwiri yokhota yomwe ili pa tchati

ikusonyeza ‘Msewu Wopita ku Moyo Wathanzi’

umene mwana ayenera kuyenda.

Mzere wa madontho ukusonyeza kulemera kwa

mwana kuchoka mwezi umodzi kufika wina,

komanso kuchokera chaka china kufika chaka

chinzake.

Kwa ana amene akukula moyenera ndi moyo wathanzi, kamzera ka madontho

kamayenda pakati pa mizere yaitali yokhotayo. Ndi chifukwa chake malo amene ali

pakati pa mizere iwiriyo amatchedwa Msewu Wopita ku Moyo Wathanzi.

Ngati kamzere ka madontho kakwera popanda kutsika, mwezi ndi mwezi, kulowera

mbali imodzi monga mizere yaitali yokhotayo, ichinso ndi chizindikiro choti mwana ali

ndi thanzi.

Mwana wathanzi, amene amalandira chakudya chokwanira chokhala ndi zonse

zofunikira m’thupi, nthawi zambiri amayamba kukhala, kuyenda, ndi kuyankhula

pafupifupi nthawi zimene zatchulidwa pansipa.

Chithunzi chenicheni cha

MWANA WATHANZI,

WODYETSEDWA BWINO

Kwa mwana wa

moyo wathanzi,

wodyetsedwa

bwino, sikelo

imakwera

mosalekeza.

Madontho nthawi

zambiri amakhala

m’kati mwa mizere

yosonyeza Msewu

Wopita ku Moyo

Wathanzi.

mwana akukhala

osagwiriridwa

mwana wa

miyezi 6

mpaka 8

wayamba kuyenda

timasitepe tingapo

mwana wa

miyezi 12

mpaka 16

wayamba

kulankhala

nau amodzi

mwana wa miyezi

11 mpaka 18

321

wayamba kunena

maganizo omweka

mwana wa

zaka zitatu

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!