17.06.2013 Views

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

Mmene Mungagwiritsire ntchito Tchati

cha Moyo wa Mwana

CHOYAMBA,

lembani miyezi ya

chaka cho

mtimabokosi

ting’onoting’ono

pansi pa tchati.

Lembani mwezi pamene mwana adabadwa

m’kabokosi koyamba m’chaka chilichonse.

Tchati ichi chikusonyeza kuti mwana adabadwa mmwezi wa Malitchi.

CHACHIWIRI, kwezani mwana pa sikelo.

Tingoyerekeza kuti mwana adabadwa mwezi wa Epulo. Tsopano ndi

Ogasiti, ndipo mwana akulemera makilogilamu 6.

CHACHITATU, yang’anani pa khadi.

Makilogalamu amalembedwa kumbali kwa khadi.

Funani pamene palembedwa makilogalamu amene

mwana akulemera (M’chitsanzo ichi ndi makilogalamu 6).

Sikelo

yozendewera

kapena ya

katungw e

319

Kenaka fufuzani mwezi umene tilimo pansi pa tchati

(m’chitsanzo chino ndi Ogasiti wa chaka choyamba cha

mwanayo).

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!