17.06.2013 Views

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

316

Kukula kwa ana komanso “msewu wopita

ku moyo wa thanzi”

Mwana wathanzi amakula mosabwerera m’mbuyo. Ngati iye adya

zakudya zokhala ndi zonse zofunikira m’thupi la munthu, komanso

ngati alibe matenda ena aakulu, mwana amalemera mowonjezera

mwezi uliwonse.

Mwana amene akukula bwino ndi wathanzi.

Mwana amene akukwera sikelo pang’onopang’ono kuyerekeza ndi ana ena, nasiya

kukwera, kapena ngati akutsika, alibe moyo wathanzi. Mwina iye sakudya mokwanira

kapena ali ndi matenda aakulu, kapena zonse ziwiri.

Njira yabwino yodziwira ngati mwana ali bwino komanso kuti akudya zakudya

zokhala ndi zonse zofunikira m’thupi ndiyo kukamukweza sikelo mwezi uliwonse ndi

kuwona ngati iye akuwonjezera kulemera moyenera. Ngati kukwera sikelo kwa mwana

kusonyezedwa pa Matchati a Moyo wa Mwana, nkwapafupi kuwona ngati mwanayo

akuwonjezera kulemera kwake moyenera.

Atagwiritsidwa ntchito bwino, matchati adzadziwitsa amayi ndi ogwira ntchito

zachipatala pamene mwana sakukula moyenera, kotero kuti angachitepo kanthu.

Akhoza kuyamba kuwonetsetsa kuti mwana akudya mokwanira, ndipo akhoza

kumthandiza pa matenda ali wonse amene mwana angakhale nawo.

Tsamba lotsatira lili ndi Tchati cha Moyo wa Mwana chenicheni chosonyeza ‘Msewu

Wopita ku Moyo wa thanzi’ Tchati chimenechi chitha kudulidwa ndi kusindikizidwanso.

Ndi chinthu chofunika kwambiri kuti amayi onse akhale ndi Matchati a Moyo wa Ana

ake onse a zaka zosafika 5. Ngati pafupi pali chipatala chaching’ono kapena

chipatala cha sikelo ya ana, mayi ayenera kupita ndi ana ake, ndi matchati awo, kuti

akakwezedwe pa sikelo ndikukawonedwa ngati akudwala mwezi uliwonse. Ogwira

ntchito zachipatala atha kuthandiza kufotokoza za patchati ndi kagwiritsidwe kake

ntchito.

Kuti musunge bwino Tchati cha Moyo wa Mwana, ikani mu enivelopu ya pulasitiki.

Kukweza sikelo ana ang’onoang’ono

SIKELO YOCHITA KUPANGA KUNYUMBA

Mutha kupanga sikelo ndi mtengo wouma

kapena nsungwi. Mlingo wolemera umene

mungagwiritsire ntchito ndi thumba, botolo,

kapena chitini chodzadza ndi mchenga.

mbedza ziwiri zotalikirana 5 cm

sikelo yalendewera ku mbedza iyi

mtengo (mtanda) wotalika 1 m

choyangata

(chonyamula)

mwana

Kulemera kwa mwana kumakhala

kokhozeka pamene mtanda uli

wapingasa molunjika kapena

mosapendekera mbali imodzi.

chinthu

chosunthikasunthika

SIKELO YOMWE

IMASONYEZA

KULEMERA KWA

MWANA MOSAPHEKA

KAPENA MOKHOZA

Chitchati cha mwana

chimaikidwa kumbuyo

kwa sikelo pofuna kuti

munthu wolembera

kulemera kwa

mwanayo asonjeza

mosalakwitsa

chiwerengero

chenicheni cha mmene

mwana walemerera pa

sikelopo.

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!