17.06.2013 Views

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

339

• Ngati mlomo wa mwana kapena m’mwamba mwa

mlomo wake ugawanika pawiri, atha kukhala ndi mavuto a

kuyamwa ndipo ayenera kumadzamudyetsera sipuni.

Mwakuchita opaleshoni wa mlomo wa m’mwamba zikhoza

kubwezeretsa mlomowo m’malo mwake. Nthawi yabwino

yochitira opaleshoni ya mlomo ndi pamene ali ndi miyezi 4

mpaka 6, ndipo miyezi 18 ngati ili opaleshoni ya

m’mwamba mwa mlomo.

Mlomo wogawanika pawiri

7. Zovuta pa nthawi yobereka nthawi zina zingachititse kuwonongeka kwa

bongo. Zimene zingachititse mwana kukhala ndi ziwalo zouma ndi zizindikiro za

kugwa khunyu. Mpata wa kuwonongekaku ndi waukulu ngati pa nthawi yobadwa

mwanayo sapuma mofulumira, kapena ngati mzamba adapereka jekeseni yofulumizitsa

kubadwa kwa mwana mwanayo asanabadwe (tsamba 282).

Khalani osamala ndi mmene mumasankhira mzamba wanu ndipo musalole

mzamba wanu kugwiritsira ntchito mankhwala ofulumizitsa kubereka mwana

wanu asanabadwe.

Mwana wa minofu yomangika (Celebral Palsy)

Miyendo yopiringidzana

kapena yopitama ngati

sizesi.

Mwana wodwala matendawa amakhala ndi minofu

yomangika ndi youuma kotero kuti satha kusuntha ziwalo

bwinobwino. Nkhope yake, khosi lake, kapena thupi lake litha

kupotoka, ndipo mayendedwe ake amadzandira. Nthawi

zambiri minofu yomangika m’kati mwa miyendo yake

imachititsa kuti miyendo yake ikhale yopachikana ngati

sizesi.

Pa nthawi yobadwa mwanayo akhoza kuwoneka ngati ali

bwinobwino kapena womasuka bwinobwino. Kumangika

kumabwera iye akamakula. Mwanayo atha kudzakhala

woganiza msanga kapenanso mochedwa.

Palibe mankhwala amene amachiritsa kuwonongeka kwa

bongo kumene kumachititsa kumangika kwa minofu. Koma

mwana afunikira chisamaliro chapadera. Pofuna kulewa

kumangika kwa minofu m’miyendo kapena mapazi, perekani

chithandizo monga cha mafupa olekana m’chiuno (tsamba 335)

ndiponso mwendo wokhota (tsamba 338), ngati kuli kofunika.

Mthandizeni mwanayo kusuntha, kukhala komanso kuima

kenaka kuyenda monga lasonyezera tsamba 334.

Mlimbikitseni kugwiritsira ntchito kuganiza ndi thupi

mulimonse mmene angathere. Mthandizeni kuphunzira (onani

tsamba lotsatirali). Ngakhale kuti iye ali ndi vuto la

kuyankhula atha kukhala ndi mphamvu yabwino ya kuganiza

ndi kutha kuphunzira zinthu zochuluka atapatsidwa mpata.

Mthandizeni kuti adzithandize yekha.

Kuchedwa kukula m’miyezi yoyambirira ya moyo wake

(Retardation)

Ana ena amene ali ndi thanzi labwino pa nthawi yobadwa sakula bwino. Amayamba

kuganiza mochedwa chifukwa sadya chakudya chokhala ndi zonse zofunikira m’thupi

la munthu. M’kati mwa miyezi yochepa yoyambirira ya moyo wawo, bongo umakula

mofulumira kuposa pa nthawi ina iliyonse. Chifukwa cha chimenechi chakudya

choyenera kwa mwana ndi chofunika kwambiri. Mkaka wa m’mawere ndicho chakudya

chabwino koposa kwa mwana (onani chakudya chabwino cha mwana, tsamba 125).

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!