17.06.2013 Views

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

338

Nkhope ya mwanayo imawoneka yefufuma, ndipo imawoneka ya tondovi, lirime lake

limayenda kunja, ndipo chipumi chonse chitha kukhala ndi tsitsi. Ngofowoka, sadya

moyenera, amalira pang’ono, ndipo amagona kwambiri. Amaganiza mochedwa ndipo

atha kukhala ogontha. Adzayamba kuyenda ndi kuyankhula mochedwa kuyerekeza ndi

ana oti ali bwinobwino.

Pofuna kuthandiza kupewa vuto lobwera kwa mwana chifukwa chosowa

mchere wa ayodini (iodine) m’thupi mwa mayi (cretinism), amayi apakati

ayenera kugwiritsira ntchito mchere wokhala ndi iodine m’malo mwa mchere

wamba (onani tsamba 135).

Ngati mukuganiza kuti mwana wanu atha kukhala ndi vuto la cretinism pitani naye

kuchipatala kapena kwa dotolo nthawi yomweyo. Kulandira mankhwala mwachangu

(a thyroid) kumatanthauza kukhalanso bwino mwachangu.

3. Kusuta kapena kumwa zakumwa zaukali pamene mayi ali ndi mimba kumachititsa

ana kubadwa aang’ono thupi kapena kukhala ndi mavuto ena (onani tsamba 156).

Osamamwa kwambiri kapena kusuta makamaka pamene muli ndi pakati.

4. Zikadutsa zaka 35, mpata ndi waukulu woti mayi adzakhala ndi mwana wokhala

ndi vuto lina lake la pathupi. Matenda a mongolism kapena Down’s disease, amene

amawoneka ngati cretinism ndi ochuluka pakati pa ana amene mayi ali wachikulire

kwambiri.

Ndi bwino kukonzeratu za ukulu wa banja lanu kotero kuti simukukhalanso

ndi ana ena pamene mupyola zaka 35 (onani mutu 20).

5. Mitundu yosiyanasiyana ya mankhwala itha kuvulaza mwana amene akukula

m’mimba mwa mayi.

Gwiritsirani ntchito mankhwala ochepa monga mmene mungathere pa

mthawi imene muli ndi pakati ndipo akhale okhawo amene mukudziwa kuti

saika moyo wa mwana pa chiswe.

6. Ngati makolo ali pachibale (pachisuweni, mwachitsanzo), pali mpata waukulu

kuti ana awo adzakhala ndi vuto lapathupi kapena adzakhala oganiza mochedwa. Maso

a ntchefu, zala zowonjezereka, mapazi okhota, mlomo wam’mwamba

wogawanika ndi mavuto a pathupi odziwika bwino.

Pofuna kuchepetsa mpata wa mavuto amenewa ndi ena, musakwatire wachibale

wapafupi. Komanso ngati muli ndi vuto lobadwa nalo lachilendolendo pa ana omwe muli

nawo, ganizirani zosiya kukhalanso ndi ana ena (onani Ndondomeko za Kulera, mutu 20).

Ngati mwana wanu abadwa ndi vuto lapathupi, pitani naye

kuchipatala. Nthawi zambiri kena kake kakhoza kuchitidwa.

• Ngati lili vuto lokhala ndi maso antchefu (cross-eyes), onani

tsamba 234.

• Ngati mwana abadwa ndi chala chowonjezereka chaching’ono

kwambiri ndipo ndi chopanda fupa m’kati mwake, chimangeni

ndi kachingwe mothinitsa kwambiri. Chotsatira chake ndi

chakuti chalacho chidzauma ndipo kenaka chidzaduka. Ngati

chili chachikulu ndipo chokhala ndi fupa, muchisiye

choncho kapena mupite kuchipatala kuti akachichotse.

• Ngati mapazi a mwana wobadwa kumene ali okhotera m’kati

kapena apanga chibonga, yesetsani kumawawongolera

monga mmene ayenera kukhalira. Ngati mungachite

zimenezi msanga, chitani zimenezi kambirimbiri tsiku

lililonse. Mapazi (kapena phazi) ayenera kukula

pang’onopang’ono kuti akhale monga mmene ayenera

kukhalira. Ngati simungathe kuwongola mapazi a

mwanayo kuti akhale m’malo mwake, pitani naye

nthawi yomweyo kuchipatala kumene mapazi ake atha

kumangidwa kuti akhale mchimake, mwakuika mu

chikhakha. Kuti pakhale zotsatira zabwino ndi pofunika

kutero m’kati mwa masiku awiri akabadwa.

Phazi

lokhotera

m’kati

Phazi lokhala

ngati

chibonga

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!