17.06.2013 Views

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

333

Ngati muli ndi maganizo oti mwana ali ndi diphtheria:

• Mgonekeni mchipinda chayekha.

• Kalandireni chithandizo cha kuchipatala mwamsanga. Pali mankhwala olimbana ndi

tizilombo toyambitsa matenda a diphtheria.

• Perekani penicillin, mbulu umodzi wa mayunitsi 400,000, katatu pa tsiku kwa ana

akuluakulu.

• Amwe madzi ofunda othira mchere pang’ono.

• Mkonzereni kuti apume mpweya wa madzi otentha kawirikawiri ndi mosalekeza

(tsamba 177).

• Ngati mwana ayamba kutsamwa ndi kusandulika buluwu (blue), chotsani kangaude

kummero kwake pogwiritsa ntchito kansalu kamene mwaveka chala chanu.

Diphtheria ndi nthenda yowopsa imene ingapewedwe mwachangu ndi katemera wa

DPT. Onetsetsani kuti ana anu alandira katemerayu.

Poliyo (Polio, Poliomyelitis)

Poliyo akupezeka kwambiri pakati pa ana osakwana zaka

ziwiri zakubadwa. Imabwera ndi kachilombo ka vairasi ngati

kamene kamachititsa chimfine, kawirikawiri ndi kutentha

kwa thupi, kusanza, kutsekula m’mimba, ndi zilonda

m’minofu. Nthawi zambiri mwana amachira kotheratu

m’masiku owerengeka. Koma nthawi zina chiwalo china

chathupi chimafowoka kapena kupuwala. Nthawi zambiri izi

zimachitika ku mwendo umodzi kapena yonse iwiri.

Pakapita nthawi mwendo kapena mkono wofowoka uja

umawonda ndipo siukula mofulumira ngati unzake uja.

Chithandizo:

Matendawa akangoyamba, palibe mankhwala amene

adzaletse kupuwalako. (Komabe, nthawi zina mbali kapena

mphamvu ina yonse imene yataika imabwerera

pang’onopang’ono.) Mankhwala olimbana ndi kupha

tizilombo toyambitsa matenda m’thupi sathandiza. Monga

chithandizo choyambirira, chepetsani ululu ndi panadolo

(paracetamol) kapena aspirin ndipo ikani nsalu

zonyowetsedwa ndi madzi otentha paminofu yowawayo.

Mkhazikeni mwanayo mwa njira yoti amve bwino ndi kuletsa

kupinda kapena kuunjikana kwa minofu ya ziwalo.

Pang’onopang’ono wongolani manja ake ndi miyendo kotero

kuti mwanayo akhale mowongoka mmene angathere. Ikani

zinsalu pansi pa mawondo ake, ngati kuli kofunika kuti ululu uchepe, koma onetsetsani

kuti mawondo ake ndi owongoka.

Kapewedwe kake:

• Katemera wa poliyo ndiye chitetezo chabwino kwambiri.

• Musapereke jekeseni wa mankhwala a mtundu wina uliwonse kwa mwana amene ali

ndi zizindikiro za chimfine, kutentha thupi, kapene zizindikiro zina zili zonse zimene

zitha kuchititsidwa ndi vairasi ya poliyo. Ululu wochititsidwa ndi jekeseni utha

kusintha poliyo yapang’ono yosapuwalitsa ziwalo kukhala yodetsa nkhawa,

yotsagana ndi kupuwala ziwalo. Musabaye jekeseni wa mankhwala ena

aliwonse pokhapokha ngati kuli koyenera.

Onetsetsani kuti ana alandira katemera wa poliyo, wa ‘madontho a poliyo’

pamene ali ndi miyezi iwiri, itatu kapena inayi yakubadwa.

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!