17.06.2013 Views

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

Ukhondo

315

Ana adzakhala ndi moyo wathanzi ngati midzi, makomo ndi iwo eni akewo ali

aukhondo. Tsatirani malangizo aukhondo amene ali m’mutu 12. Aphunzitseni ana anu

kuzitsatira ndi kuzimvetsa ubwino wake. Pano malangizo ofunika kwambiri

abwerezedwa.

• Asambitseni ana anu ndi kuwasintha zovala zawo nthawi zonse.

• Aphunzitseni ana kusamba m’manja nthawi zonse pamene adzuka m’mawa,

akachoka ku chimbudzi, komanso asanadye kapena kugwira chakudya.

• Kumbani zimbudzi ndipo aphunzitseni anawo kuzigwiritsira ntchito zimbudzizo.

• Kumene kuli mahukuwemu, musalole ana anu kuyenda opanda nsapato; gwiritsirani

ntchito nsapato.

• Phunzitsani ana kutsuka mano ndipo musamawapatse mabisiketi ambiri, maswiti

kapena zakumwa monga kokakola.

• Dulani zikhadabo zawo kuti zikhale zazifupi.

• Musalole ana amene ali odwala kapena amene ali ndi zilonda, mphere, nsabwe,

kapena chipere kugona ndi ana anzawo kapena kugwiritsira ntchito zovala zimodzi

kapena nsalu yopuputira.

• Apatseni chithandizo msanga ana amene ali ndi mphere, chipere, njoka

zam’mimba, ndi matenda ena opatsirana mosavuta kuchoka kwa mwana wina

kupita kwa mwana m’nzake.

• Musalole ana anu kuika zinthu zakuda m’kamwa kapena kulola galu kuwanyambita

nkhope zawo.

• Musalole nkhumba, agalu, ndi nkhuku kukhala m’nyumba mwanu.

• Musaike zakudya za ana m’mabotolo, chifukwa amavuta kutsuka kwake ndipo

zikhoza kubweretsa matenda. Apatseni makanda mkaka wa m’mawere kuchokera

mu kapu kapena ndi sipuni.

• Gwiritsirani ntchito madzi otetezedwa kapena owiritsidwa monga akumwa. Izi

nzofunikira kwambiri kwa makanda.

Katemera

Makatemera amateteza ana ku matenda ambiri

amene ali owopsa kwambiri kwa ana monga chifuwa

chokoka mtima, diphtheria, kafumbata, matenda

opuwalitsa ziwalo, chikuku ndi chifuwa chachikulu.

Ana ayenera kupatsidwa makatemera

osiyanasiyana miyezi yoyambirira ya moyo wawo,

monga tsamba 154 lasonyezera. Katemera wa

matenda opuwalitsa ziwalo a poliyo ayenera

kuperekedwa koyambilira pasanathe miyezi iwiri,

chifukwa matenda opuwalitsa ziwalo ndi ochuluka

pakati pa ana osapitirira chaka chimodzi.

Chitani izi

Pofuna

kuteteza

izi

katemera wa poliyo

Zofunika kudziwa: Kuti mwana atetezedwe

mokwanira, makatemera a DPT (diphtheria, chifuwa chokoka mtima, kafumbata) ndi

poliyo ayenera kuperekedwa kamodzi pa mwezi kwa miyezi itatu ndiponso kamodzi

chaka chinacho.

Kafumbata wa mwana wongobadwa kumene atha kupewedwa powapatsa amayi

katemera wa kafumbata pa nthawi imene iwo ali ndi pakati (onani tsamba 266).

Onetsetsani kuti ana anu akulandira makatemera onse amene akufunikira.

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!