17.06.2013 Views

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

Kodi tingachite chiyani kuti titeteze moyo wa ana?

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

TCHATI CHA MOYO WA MWANA CHOSONYEZA MOYO WENIWENI WA MWANA

Mwanayu anali wathanzi Ali ndi miyezi 6, mayi Ali ndi miyezi 10 anayamba Ali ndi miyezi 13

ndipo amakwera bwino sikelo adapezekanso ali odwala ndipo kutsekula m’mimba ndipo mayi ake adaphunzira

miyezi yoyambirira 6 ya moyo adasiya kumuyamwitsa. Adayambanso kutsika sikelo. Ubwino wompatsa

wake, chifukwa choti mayi Mwana adayamba kudya tinthu adawonda ndi kudwala chakudya choyenera.

ake ankamuyamwitsa. tosakwanira monga chimanga kwambiri. Sikelo yake inayamba

ndi mpunga. Adasiya kuwonjezera kukwera msanga. Ali

kulemera. ndi zaka ziwiri anali

akuyamwa

akunenepa

bwino

kusiyana kuyamba

pa miyezi 6

sakudya

bwino

sikelo ikukwera

pang’ono

kutsekula m’mimba

kuyambika pa

miyezi 10

akuwonda

akutsekula

m’mimba

kudya zakudya zathanzi

kuyambika pa miyezi 13

ali pa msewu Wopita

ku Moyo wa Thanzi.

akunenepa

bwino

Matchati osonyeza moyo wa mwana ndi ofunika. Atagwiritsidwa ntchito bwino,

amathandiza amayi kudziwa pamene ana awo akufunikira kwambiri zakudya

za kasinthasintha ndi chisamaliro chapadera. Amathandiza ogwira ntchito za

chipatala kumvetsa bwino zosowa za mwana ndi banja lake. Zimathandizanso mayi

kudziwa pamene wachita ntchito yotamandika.

323

wodyetsedwa

bwino

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!