28.02.2013 Views

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

ZOCHITA SABATA LINO:

Tsiku 1: Tapiman umoyo wa maphemphero anu ndimafunso aya.

! Kodi mumapemphela kangati ?

! Kodi muma pempherera zinthu zotani?

! Kodi mau ena amene mumalankhula mupemphero lanu yataya tanthauzo

! ! chifukwa cho wasewendzetsa panthawi yaitali ?

Tsiku 2: Lolani pemphelo kuti ikhale yopambana pa nchito zautumiki zanu zonse

! sabata lino, popemphelani mʼmaba, msana ndi usiku sabata lino. Kodi

! muzakwanilitsa bwanji nchito imeneyi?

Tsiku 3: Muzamapemphero anu, pempherani, ndi mapempho a umunthu ndiponso a

! Umulungu. Pempherani mu mzimu ndiponso ndi mu umuthu wanu (1 Akorinto

! 14:15).

Tsiku 4: Pempherani tsiku ndi tsiku kuti Mulungu atume “okolola za mʼmunda” (Luka

! 10:2) ndiponso kuti ndanga yopeleka ulaliki wa uthenga wa chiyembekezo

! uonekele. the Gospel and make disciples. Gulu la Atsogoleli a Strategic Impact

! onse ama ika chikumbuso cha nthawi ya pa 10:02 AM pa mafoni yao ndipa ma

! Alamu tsiku iliyonse kuti apempherere okolola zamʼmundat. Chonde tipempha

! kuti muchite chimodzimodzi.

! 47

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!