Create successful ePaper yourself
Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.
! Chachiwiri, ifeyo tisa pemphere monga ngati “achikunja” - upemphera ndi mau

yochulukila koma yopanda tanthauzo. Uko ndiko kupemphera kogabikana ndi

kosachokela pansi pamtima. Nthawi zambiri tima zipangila pemphero yomwe

timapemphera nthawi yonse ngati mwachizowerezi ndi ku iwala tanthauzo

yapoyamba. Mwachisoninso, ngakhale pemphero ya chitsanzo ya Ambuye Yesu

yakhali ngati imodzi ya mapemphero yamʼtunduyu. Mau yakhala ngati yalibe

tanthauzo iliyonse. Akristo safunika kupemphera ndi mau yopanda tanthauzo,

ubwebweta bwebweta chabe ndiku chulutsa mau kuti Mulungu atiyankhe. Iyai !

Ndime 8 iti uza kuti Mulungu amatimva. Atate adziwa zonse zimene tizifuna TIKALIBE

kuti tipemphere! Mulungu ndi wamʼkulu, choncho ngati tiku pemphera kulibe chimene

Mulungu sanachidziwe kale.

NDEMANGA/MAFUNSO: Kodi tingapewe bwanji mapephero yo bwerezela ndiyopanda

" pindu yomwe Ambuye Yesu anati chenjenza?

! Pakuti Mulungu aziwa zonse zomwe tikufuna nichifukwa ninji tifunika

upemphera? Zifukwa ndizambiri zomwe tifunikila upemphera: 1) Tinalamulilidwa -

ndiku mvelela Mulungu. 2) Chosonyeza zofunikila zenizeni za moyo wathu –

pachifukwa chakuti iseyo tipemphera chimvumbulutsa kuti zofunika koposa ndiziti pa

umoyo wathu. 3) chitsonyeza udalila kwathu – ise ngati tikubwera kwa Ambuye ndiku

peleka mapephero yathu tiku sonyeza kuti ti dalila iye kuti ndiye amatipasa zonse.

Chachikulu ndi ichi, 4) chiyanjano chatu ndi Mulungu chipita patsogolo – chiyanjano

ndi Mulungu chimachokela pomwe tikhala pomodzi ndi Abuye. Kuchuluka kwa nthawi

yomwe ti khala ndi Mulungu mumapephero ndi kuwerenga mau tizakhala pafupi nae.

Timudziwa bwino Mulungu.

NDEMANGA/MAFUNSO: Kodi Uopemphera kwaku nthandizani motani kuti inu mukule

" mchiyanjano chanu ndi Mulunguow?

PEMPHELO LA CHITSANZO:

! Mu buku la Mateo 6:7-13, Ambuye Yesu anatipatsa chitsanzo mo pempherera.

Tipeza zibvumbulutso zambiri momwe Yesu anali ku pempherera ndi zinthu zomwe

anali kupepherera. Choyamba, apemphera ndi nzelu. Osati ngati munthu ali

kupemphera kwa mulungu wakutalitali koma ngati kwa Mulungu ali pafupi ndiponso

amene ali Tate wathu. Osati Tate wina chabe koma Tate wathu wa Kumwamba

chichiwiri, Yesu anali upemphera pamodzi ndi ena. Yesu anali kuzi pempherera

ndiponso anapemphreranso Akristu panthawi imodzi. Chachitatu, ana pemphera ???

kwa Mulungu yekha.

! 45