28.02.2013 Views

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

ZOCHITA SABATA LINO:

Tsiku 1: Wkodi ndi anthu oti amu gulu lanu omwe azakuthandizani kuti mukwanilitse

! maso mpenya yopereka uthenga kudziko lanu lonse ndi kubyala mipingo

! yatsopano padziko lonse lapansi? Talembani ma ina ya anthu ali mu gulu lanu.

! Ngati mulibe gulu pempherani kuti Mulungu aku patseni ma ina ya athu omwe

! munga sewenza nao.

! ! 1. _______________________________________

! ! ! 2. _______________________________________

! ! ! 3. _______________________________________

! ! ! 4. _______________________________________

! ! ! 5. _______________________________________

Tsiku 2: Sankhani nthawi yomwe inu ndi gulu lanu lidza kumana kuti mubalalitse maso

! mhenya yopereka ulalika kwa onso amitundu ndi kuchulutsa ophunzila.

! Ganizilani mosamala zomwa muza lankhula nao. Talembani maganizo yanu

! pansipa:

Tsiku 3: Pomwe muli kusiliza chigawo choyamba cha Sikulu Yochulutsa Atsogoleli

! (maphunzilo kumi yoyamba), inu mwapephedwa kuti muphunzitse azitsogoleli

! atsopano Awiri kapena Asanu kapena kusewenzetsa buku limeneli. Kodi ndiliti

! pomwe mozayamba ukumana ndipo ndi nthawi yanji?

! Liti: ______________________________________________________

! Kuti: ______________________________________________________

Tsiku 4: Ndimbali iti la mzinda wanu yomwe inu ndi gulu lanu latumidwa ndi Mulungu

! kuti mukapereke ulaliki?

! 43

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!