28.02.2013 Views

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

6. Zolungamika pakati pa maphunzilo:

! Kamodzi pa mwezi, kamodzi minyezi itatu iliyonse kapena makamaka kamodzi

! pa chaka:

! PIMANI ngati mukupita patsogolo ngati gulu. Mukumane ndi gulu lanu ndi

! kufunsa, “kodi ndi zotani zomwe tifunika usintha kuti tikwanilitse ku itanidwa

! kathu ndi Mulungu?”

MOTSILIZA:

Zinthu zitatu zofunika kuti tikhali opanga Ophunzila ampamvu:

1. Aphunzitsa afunikila Hkuti akhale ozindikila ndi kudziwa zomwe afunika

ophunzila kuti amudziwe Mulungu. Azafunika udziwa zofunika pa umoyo wa

ophunzila.

2. He must have a clear picture of what he wants these disciples to become. He

must know what bedrocks elements of Christian character must be developed.

3. He must have a vivid vision of what he wants them to learn to do, and a

workable plan to help to accomplish it.

NDEMANGA/MAFUNSO: Lingo la Strategic Impact ndi kuphunzitsa ATSOGOLELI amene

" aza phunzitsa atsogoleli ena kuti achulutse Ophunzila amene aza peleka

" uthenga wa Ambuye Yesu ndi ku chulutsa mipingo. Pomwe tikutsiliza maphunzilo

" yathu yoyamba (maphunzilo khumi), tikupempa yense wa inu kuti abweretse

" azitsogoleli astopano awiri kapena atatu omwe inu muzaphunzitsa

" kusewenzetsa bukuli. Muzakumana kamodzi sabata iliyonse kuti muphunzilenso

" zomwe muna phunzila kale pamenenso inu mukupitiliza ndi gulu lanu loyamba.

! Nichifukwa ninji ndi cho funikila kuti tiphunzitse ena?

! Kodi mzinda wanu uzasintha motani ngati ophunzila akuchulukila?

! 42

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!