28.02.2013 Views

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

NDEMANGA/MAFUNSO: Kulingana ndi mau aya Mako 3:14, kodi lingo loyamba lomwe

" Mulungu ana itanila inu ndi a Kristu ena? Kodi chimenechi chitanthauza chiani

" kwa inu ndi Agulu lanu pakhani ya zofunikila?

" Yesu akalibe usankha Atumwi ake khumi ndi awiri, ana pemphera usiku onse

" kwa Mulungu (werengani Luka 6:12). Kodi mwakhala mukupephera kuti Mulungu

" “Atume okolola zamʼmundaʼ? (Luka 10:2)

3. Sonyezani maso mphenya:

! Lembani mundandanda wa anthu omwe mukhulupirira kuti Mulungu akuku

! tumani kuti musewenze nao, ndikuwa takasa kuti asewenze pamodzi ndi inu kuti

! akwanilitse nchito yopeleka uthenga kwa amitundu.

NDEMANGA/MAFUNSO: Kodi mungakope bwanji mitima za ena kuti asate maso mpenya

" yanu?

4. Pangani njila kapena mapulano ndi ku gawa zinchito kuti inu mu kwanilise

nchito yopeleka uthenga ku mzinda wanu/ndziko lanu/dela lanu/ ndi dziko

lonse lapanse:

! Sankhani zithu zitatu zofunikila zomwe muzachita tchaka chino t

! Gawilani anthu zi nchito zomwe aliyense membala yamu gulu afunika kuchita

! kuti mu kwanilise maso mpenya.

5. Pimani za phindu:

! Pamene enu ndi agulu lanu aku sewenza nchito ya ulaliki ndi chofunika kuti

! mupime za mpindu zomwe zikuchitika. (werengani Luka 10:1, 17). Ichi chi

! tanthauza kuti mufunika ku zi ikila chipimo cha zochita zomwe Mulungu

! azakutsogolelani.

NDEMANGA/MAFUNSO: Kodi muzaziwa bwanji ngati mukupita patsogolo kuti mu kwanilitse

! maso mpenya yanu?

! 41

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!