Create successful ePaper yourself
Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.
STRATEGIC IMPACT - SUKULU YOCHULUTSA AZITSOGOLELI

PHUNZILO 9 - UBYALA MIPINGO

“MFUNDO 3 & 4: SONKHANITSANI NDI KUPHUNZITSA OPANGA OPHUNZILA”

Pamene muyamba ukumana, gawanikani mʼmagulu ya anthu ANAI pagulu limodzi

pampindi zokwanila ngati makumi yatatu mwina mwache mochepekela.

Muphephererani wina ndi mzache ndipo mufunsane mafunso ya ungwilo. Pambuyo

pache nkhalaninso mʼmagulu anu ndiku werenga phunzilo ili ndiku ponyapo

ndemanga.

Mphunzitsani GULU, osati chabe “Mtsogoleli”

! Mtsogoleli wachi kristu aliyese ali kuchita zazikhulu padziko lapansi, sachita

zimenezi payekha ai. Yesu Kristu anali ndi ʻguluʼ la atumwi khumi ndi awiri amene iye

ana phunzitsa ndi ku wutuma padziko lapansi. Mtumwi Paulo anali ndi gulu lakenso.

Sanachite utumiki payekha. Ngati mukufuna ukwanilisa ku itanidwa kwa Mulungu pa

umoyo wanu ndi bwino kuti mumange gulu lo chulukitsa Ophunzila amene ali

ozipereka ku utumiki wa mau pa dziko lapansi. Lingalilani izi po sonkhanitsa ndi

kuphunzitsa gulu lanu;

1. Zindikilani maso mpenya ya Mulungu pa umoyo wanu.

! Malemba yakuti pa nkhani ya Davide, “pamene Davide ana tumikila lingo la

! Mulungu kwa mʼbadwe wake kulingani ndi chifunila cha Mulungu, ana

! mwalila.” [Acts 13:36]

! Kulibe mau yabwino yopambana aya kuti yakalankhulidwe pa imoyo wathu - kuti

! tina kwanilitsa chifunilo cha Mulungu mu ʻbadwo wathu! Inu simunalengedwe ai.

! Sichangozi kuti inu ndinu mwana wa Mulungu pa nthawi ino ndi pamalo pomwe

! mukukhala. Mulungu ali ndi lingo lalikhula pa umoyo wanu. Ana ku itanani kuti

! muchite chifunilo chache!

NDEMANGA/MAFUNSO: Nichifukwa ninji Mulungu ana ku ikani padziko lapansi pa

" nthawi ino?

" Kodi ku itana kwa Mulungu pa umoyo wanu mukukudziwa?

" Kodi chomwe mukufunisisa pa umoyo wanu chopambana zonse ndi chiani?

2. Mupepheni Mulungu kuti abweletse Anthu okuthandizani kuti mukwanilitse

Maso Mpenya yanu.

! Mako 3:14 itisonyeza momwe Yesu anasankhila gulu yake kuti akwanilitse lingo

! lache padziko lapansi.“ndipo anasakha khumi ndi awiri kuti akhale nao , andi

! kuwa tuma kuti akalalike uthenga wa Mulungu.”

! 40