You also want an ePaper? Increase the reach of your titles
YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.
STRATEGIC IMPACT - SUKULU YOCHULUTSA AZITSOGOLELI

PHUNZILO 8 - UTUKULA UTSOGOLELI

“CHIKHALIDWE: ZOFUNIKILA PA UMOYO WA MTOGOLELI”

Pamene muyamba ukumana, gawanikani mʼmagulu ya anthu ANAI pagulu limodzi

pampindi zokwanila ngati makumi yatatu mwina mwache mochepekela.

Muphephererani wina ndi mzache ndipo mufunsane mafunso ya ungwilo. Pambuyo

pache nkhalaninso mʼmagulu anu ndiku werenga phunzilo ili ndiku ponyapo

ndemanga.

! Mtsogoleli anga khale ndi maso mpenya yayakhulu ndi mchango koma kuli

chikhalidwe chichikulu chomwe afunika ukhala nacho, afunika ukhala okhulupilika.

Chilibe kanthu ngakhali kuti mstogoleli ali ndi mchangu ndi maso mpenya yampamvu

koma ngati sakhulupirika zonsezi zili mwachabe, anthu sadzalondola mtsogoleli otele!

Ngati mstogoleli mataya chikhulupililo cha anthu, anthu saza mulondola. Choncho

ngati mtsogoleli wa umulungu akufuna utakasa ina ndiku kwanilisa maso mpenya yaya

kulu ndibwino kuti akhale ndi CHIKHALIDWE chabwino.

! Kodi chikhalidwe ndi chiani? Chikhalidwe ndi ku khulupirika komwe kumabwera

kamba ka kusonyeza.

! Modzi wa atsogoleli ampamvu mu Baibulo ndi Mfumu Davide. Nichifukwa ninji

anali woposa? Masalimo 78:72 itipasa yankho. “And ndipo Davide ana tsogolela ndi

mtima wa mtima wa Ungwilo ndi manja ya luso.” Davide sana tsogolele chabe ndi luso

komabe anasonyeza ukhulupirika. Ukhulupirika ndiku nkhala okwana ndipo

osagawikana.ʼ Ndiku khali ukhulupirika ndipo opanda chinyengo kapena

kunyalanyaza. Munthu okhulupilika ndi munthu amene ali oyela mtima. Sasintha

pomwe ali okha ndi pmwe ali pakati ka anthu. Ndi okhulupirika ndiponso odalilika.

Achita zomwe alankhula ndipo asonga mau yao. Munthu wa ungwilo kapena

okhulupilika siuja munthu wamene alibe chilema kapena banga kapena wamene

sachimwa ai. Ichi sichotheka ai. Komabe ndi munthu wamene avomeleza ngati alakwa

ndi ku ululila machimo yake. Chifukwa chakuti asonyeza ukhulupilika nthawi zonse,

ena aphunzila ndi ku dalila iwo.

NDEMANGA/MAFUNSO:

1. Nichifukwa ninji chikhalidwe kapena ungwilo chili chofunika kwa atsogoleli a

umulungu?

2. Nichifukwa ninji chikhalidwe chosa yeluzika ndi cho optsa osogoleli wa chikristu?

3. Ndi njila zotani zomwe mtsogoleli wa chi kristu kusonyeza kuti ndi okhulupilikay?

! 38