28.02.2013 Views

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

! Chachitatu - ndipo chopambana - ndi Akugwilitsa nchito ndime yamalemba

yomwe tawelenga mu Baibulo. Njila imodzi yogwilitsila nchito ndiku sewendzetsa njila

zinai zomwe Paulo ana nena kuti ndiyo lingo lomwe Mulungu anati pasila malemba- -

“Uphunzitsa, kudzudzula, kukonza cholakwa ndi kulangiza za chilungamo,” (2

Timoteyo 3:16). Zomwe mwa phunzila, gwilitsani nchito malemba awa pa zocita mu

umoyo wanu paku sewenzetsa njila izi:

NDEMANGA/MAFUNSO: Nchifukwa chiani muganiza kuti njila iyi ya chitatu,

" “KUGWILITSA NCHITO”, ndi yo yenela kopotsa pa ku phunzila Baibulo?

ZOCHITA

Uphunzitsa: WKodi Ndizoonadi zotani Kudzudzula: kodi chomwe ndi khulipirera

zomwe Mulungu amagwilitsa nchito kuti ndi cholakwika ndi chiti? Chifukwa

zomwe inenso nifunikila kugwilitsa nchito. ninji? Kodi maziko yachiganizo kapena

chikhalidwe ichi ndichiti?

Kuphunzitsa mchilungamo: kodi ndinga

tukule bwanji mbali iyi yamoyo wanga?

Kodi ndinga yambe bwanji maganizo

kapena machitidwe achikhalidwe

chatsopano?

Lankhulani ndi Mulungu pabou pazomwe

Iye afuna kuti muchite ndi kulemba

ndmundandanda wa zomwe muzachita?

Kulungamitsa cholakwa: kodi ndizatani?

Kodi ndiza lungamitsa bwanji chikhalidwe

kapena chichitidwe ichi choipa?

Ndime yaikulu yakuti mukumbuke:

ZOCHITA SABATA LINO:

Phunzilo (Yanganilani, Matsulilani, Chitani) 2 Timotoye 2:1-7 kusewnzetsa dongotsolo

ya pamwamba.

! 37

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!