28.02.2013 Views

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

NDEMANGA/MAFUNSO: Ngati gulu werengani pamodzi 2 Timoteo 2:1 ndiku fufuza za

" mafunso aya.

PENYETSETSANI

Ndi anthu oti amene ali kuchulidwa

(Mlembi, owerenga, ine nkhani)?

Ndizotani zikulankulidwa pa za Mulungu,

Yesu Kristu kapena Mzimu Oyera?

Kodi pali lamulo kapena lonjezo?

Kodi zimenezi zichitikila kuti? Kodi zimenezi zina chitika liti?

Kodi zinthu ziku chitika motani?

(penyetsetsani kasewenzetsedwe ka mau) (penyetsetsani, njila, lingo ndi zifukwa)

Chifukwa ninji zimenezi ziku chitika?

(tafufuzani zifukwa zomwe olemba ana

lembela zimenezi ndi zonse zosatila?)

Mutu wa ndime iyi ndi uti? Ndi zotani

zomwe zanachitika patsogolo ya malemba

aya?

Kodi kuli kulinganisa kapena kusiyana? Pali mau yaliyonse yomwe

yabwerezedwa?

Zina zache zimene mwa ona Ikana zonse zimene mwa ona

mwachidule:

! 35

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!