28.02.2013 Views

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

ZOCHITA SABATA LINO:

Tsiku 1: Sabata lino,pemphelani tsiku ndi tsiku kuti ambuye akweze anchito popeza

! kuti munda wakula anchito apelewela. Panthawi 10:02 mʼmawa, onani zi gao izi

! pamene mulikutsiliza tsiku lililonse.

Sondo Loyamba Chibili Chitatu Chinai Chisanu Chibelu

Tsiku 2: Ikizani nthawi ndi aKristo ena kuti apemphelele ufumu wa Mulungu upite

! patsogolo - ndi Kupempelela a nchito kuti uthenga wa ulaliki upite kwa osowa,

! pezani danga ya kuti inuyo mupereke ulaliki. Pemphererani osowa ndiku

! pepherera nshito ya ulaliki kuti ipite patsogolo.

! Malo: _____________________ Tsiku: _____________ Nthawi:_________

Tsiku 3: Ikizani nthawi yomwe inu ndi anthu amʼgulu lanu kuti ayambe kupemphera

! ndi kuyendala malo mwa pephero – yendelani malo yomwe mufuna ku byalamo

! mpingo kuti Mulungu atsagule mitima za anthu. Pemphereraninso zonse zosowa

! ndi zo vuta mʼdelalo

! Malo: _____________________ Tsiku: _____________ Nthawi:_________

Tsiku 4: Ndi njila zina zotani zomwe munga sewenzetse kuti anthu anu akhali anthu

! apemphero?

! 32

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!