28.02.2013 Views

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

! Pemphero, tsono, ndi chida cha mpamvu kwambiri. Pemphero isonyeza uzi

chepetsa ndi kudalila mpamvu za Mulungu. Pemphero isonyezanso kuti tidalila u

lemelelo wa Mulungu ndi mpamvu yache kuti lingo lache lichitidwe. Pamene ti

pemphera, tisonyeza chiyamiko pa nchito yomwe Ambuye yesu anachita pamtanda.

Pemphero isonyedza kui MULUNGU ndiye amene amatipasa zonse za umoyo

ndiposo tipeza njila momwe tingamulimekezele po limbisa Ophunzila azathu ndi ku

panga ophunzila ena.

! Mbali zonse za utumiki wathu zifunika udzadzidwa ndi pemphelo. Ifeyo tili

ozipereka ku pemphero , koma siti tanthauza kuti timapemphera chabe. Tisa chite

kanthu kalikonse popanda ku pemphera kwa Ambuye. Tika ika zonse mʼmanja ya

Mulungu, ndipo pomwe tinga pite patsogolo mwa chitsimikizo kuti Iye azati tsogolela.

NDEMANGA/MAFUNSO: Kodi ndizinthu zotani zomwe mukuchite zomwe mukuganizila

" kuti mwenamwache mufunikila kuti mu pempherereponso mwa ka nthawi?

! Modzi ya mapemphero yomwe tiyenera kupemphera ndi kupempherera Anchitor

workers. Mubuku la Luka10:2-3, Yesu anauza ophunzila bake kuti, “The harvest is

plentiful, but the laborers are few. Therefore pray earnestly to the Lord of the harvest to

send out laborers into his harvest. Go your way; behold, I am sending you out as

lambs in the midst of wolves.” Anauza ophunzila bake kuti apempherere Anchito, ndiku

watumanso iwowo PAMENEPO! Tipempherera anchito koma sitikhala tikudikhila

anchito kuti abwere tisane yambe nchito ifeyo. Kuti nchito ya ulaliki ikwanilitsidwe

ambili anchito azachokela mzokololazo! Ganizilani mau aya pampindi imodzi yokha.

Ambila mwa iwo omwe azatengako mbali ku nchito yopereka uthenga kwa amitundu

akalibe kuti amʼzindikile Yesu ngati Mʼpulumutsi wao! Choncho , pomwe tikupempha

Mulungu kuti atume anchito, tikupempha kuti anthu osowa amʼdziwe Yesu – kuti

tipanga ophunzila! TIFUNIKA UPEMPHA! Tifunika ulandila malamulo ku chokela kwa

Ambuye! Tifunika kusewenza ndi mphamvu Zache, osati zathu ai. TIFUNIKA KUZI

PEREKA KU MAPEMPHERO, ndiku sonkanitsa Anthu athu kuti achite chimodzi

modzi! Ambili mwa ise tina ika nkholoko zathu za Alamu panthawi ya 10:02 mʼʼmawi

kuti tipempherere otuta za mʼmunda kulingana ndi Luka 10:2.

NDEMANGA/MAFUNSO: Ta imani pompa ndiku lola anthu onse amʼgulu lanu kuti aike

" Nkoloko zao kapena ma selo foni yali ndi ma Alamu pa nthawi ya 10:02 mʼmawa.

" Pemphererani panthawi iyi kuti Mulungu atume okolola zamʼmunda!

! Yesu ali ndi ulamulilo onse wa padziko lakumwamba ndi dziko la pansi.

Talamulilidwa ndi iyi kuti tipelike uthenga kwa amitundu onse. Pemphani Mbuye wa zo

kolola kuti atume otuta zamʼmunda! Indetu Zinthu zonse ndizotheka ndi Mulungu

(Matteo 19:26)

! 31

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!