28.02.2013 Views

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

ZOCHITA SABATA LINO:

Tsiku 1: Muphunzilo laciwili tina kufunsani kuti muontsele masomphenya anu

! momasukila monga kuti Mulungu ali kukuitani (p. 11). PleaseOnetselani zomwe

! muna lembamo mwina pali zomwe mungatsintemo. Kodi masompenyawo

! angnenedwe ndi mau amodzi? Kodi nkwapafupi kwa ena kuwadzindikila?

! Kodi wina angathe kuwamasulila mulunjika powamva kamodzi ?

Tsiku 2: Nchito ya kukuza choling a ndi njila yothandizila kufikilitsa masompenya

! anu. Kodi ndi njila yotani yomwe mungatele kuti mufikilitse masomphenya

! anuwo?

Tsiku 3: Kodi ndi zinthu zotani zofunikila kwainu zomwe mungathe kucita kuti

! mufikilitse masomphenya anu pa matsiku ali mukudza 30? Kodi mudzacita

! zimenezi liti? Kodi mudzazicita bwanji?

Tsiku 4: Kodi ndi anthu wotani womwe mufunika kugawana nao njila ndi

! masomphenya anuwo? Kodi mudzacita liti zimenezi? Kodi padzakhala pa unyinji

! wa anthu kapena umodzi ndi umodzi? Ikidza mitsonkhanozi mosachedwa

! konse ?

! 29

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!