28.07.2013 Views

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

Adzichitira ulemu nyumba ya Mulungu.

To respect God's house.

Alangizi apitirize kulimbikitsa kuti kubvinidwa kotereku kukukhadzikitsa uChewa wake

komanso chiKhristu chake. Ndipo khalidwe lake losinthika lidzakhala umboni kwa atsikana

ena kuti nawonso afune kubwera kwa Yesu ndi ku mpingo wake.

The instructresses need to emphasize to the initiate that going through this Christian chinamwali establishes her

identity as a Chewa woman, and as a Christian. Her changed behavious should be a testimony to her friends so

that they will also desire to come to Jesus, to join his church, and to go through the Christian chinamwali.

Potsiriza peni peni apempherere namwali kuti Mulungu amuteteze ndi kumuthandiza

adzisunge mpaka akalowe m'banja. Wopemphera amusanjike manja namwaliyo

pomupempherera. Kudya ndi kumwa onse pamodzi ndi kubalalikana zitseke zonse.

Alangizi ndi aphungu amuperekeze namwaliyo kwawo nthawi yakurnmawa, ndipo amwaliyo

atafundira nsalu kumutu kwache. Adziyimba nyimbo iyi:

At the end the initiate should be prayed for that God should protect her and help her to remain pure until

marriage. The one praying should lay hands on the initiate. Eating and drinking together should end the

ceremony after which people can disperse. The instructresses and the tutors should escort the girl home while

singing:

18. Mtetezi wanga Yesu

Mtetezi wanga

My protector is Jesus

My protector

Wotsogolera nyimbo adzisintha sintha mawu ndikuikira wena monga 'momboli wanga, ,

'mchiritsi wanga,' 'ndimbuye wanga.' Akalandiridwa kunyumba alangizi apemphererenso

mtsikana pamodzi ndi makolo ake, kuyamika Mulungu chifukwa cha mwambo wonse

umene mtsikana walandira.

The leader should be mentioning all that Jesus is, such as 'my saviour,' 'my healer,' my lord,' and so on. At

home the instructress should pray with the girl and her parents thanking God for the ceremony and the

instruction the girl has received.

Sabata yotsatira, panthawi yamapemphero payenera kukhala kamwambo kochepa

kumulandira mtsikana ku mpingo. Amfurnu aitanidwe kudzaonerera. Potsiriza mapemphero

pakhale chiyanjano ndi kumwa thobwa pamodzi kusonyeza umodzi wa anthu.

The following Sunday, during the worship service, there could be a small ceremony to introduce and

incorporate the young woman to the wider society. The chief or his representative should be invited to the

worship. A drink of sweet beer should be served at the end of the service to symbolize an act of fellowship

while embracing into the corporate body offaith.

212

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!