FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:
FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:
FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:
Create successful ePaper yourself
Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.
Amayiwo ayenera kusonyeza ntchito yake ya chiwalo chochulidwacho. Koma akachula

ziwalo za chinsinsi, azisonyeza pongodikhula mwaubwino. Ayenera kumubvinitsanso

namwaliyo.

Chiphunzitso chake ndi chomwecho chakudzisunga osadzidetsa mpaka adzakwatiwe.

Chiwalo chiri chonse chiyenera kugwiritsidwa ntchito molemekeza Mulungu.

The women demonstrate the use ofthe part that is mentioned, such as leg for walking. But for the private parts,

they should demonstrate by shaking their waist up and down. They should let the initiate dance also.

The teaching is still on sexual purity until marriage. Each part ofthe body should be used to honour God.

Chiphunzitso chotsatirachi chipangidwe musewero. Ndilokhuza atsikana awiri kapena atatu

amene akuphunzira kumachokera pakhomo pamakolo awo.

The following instruction should be acted by two to three girls who are day schooling and are staying with their

parents.

Atsikanawo akaweruka kusukulu, mmodzi amabwerera kunyumba, koma

enawo amayamba kucheza ndi anyamata nkumakafika mochedwa kunyumba.

Makolo awo akawafunsa amati amagwira ntchito tasukulu. Patapita nthawi,

mmodzi wapezeka ali ndi pakati nasiya sukulu. Mnyamata wake adaikana

mimbayo. Mtsikanayo anabvutika nayo mimbayo popezanso makolo

amtsikanayo anaipidwa nazo. Mwana atabadwa, mtsikanayo amangodwala

dwala ndipo mayi wake analibe nthawi yomuthandiza, popeza anali mayi wa

bizinesi. Mtsikanayo amangosilira rnzake uja atatsiriza sukulu mpaka

kumanga ukwati ku mpingo. Kudwala kudapitirira mpaka kumwalira, kusiya

mwana wakhanda. Pamaliropo anthu amangofunsana kuti 'Kodi ameneyu

sadamwalire ndi matenda amasiku anowa a EDZI?'

After school, one girl goes straight home while the other two go somewhere else with their

boyfriends and reach home later. When their mothers ask them why they always come later,

they say they were doing some work at school. After sometime, one girl becomes pregnant

and stops school. The boy refuses responsibility and gets away with it. The girl is very upset

and sad about it but she can't do anything. Her parents also are angry with her. After having

a baby, she is always sick, and her mother, a business woman, has no time to take care ofher

and the baby. She envies her friend who fInished school and wedded in church. Her health

deteriorates and she dies, leaving the baby. At the funeral people were asking each other

'Did she not die ofthis deadly disease called HIV/AIDS?'

Potsiriza atsikana onse adaimba, akuzungulira, ndikugwedeza mapewa kusonyeza kukana.

They end by singing while going round and moving their shoulders demonstrating refusal:

17. Ine toto, ine toto

Ine, toto AIDS ndaikana

Mankhwala sikondomu, ine toto

AIDS ndaikana

Mankhwala nkuziletsa,

Kudziletsa annanu, kudziletsa

AIDS ndaikana.

Me no no, me no no

Me, no no AIDS I have refused it

Medicine is not condom, me no no

AIDS I have refused it

Medicine is self-control,

Self-control children, self-control

AIDS I have refused it.

Alangizi alongosolele bwino bwino za kuopsya kwake kwa matenda opatsirana kudzera

muchiwere-were monga chizonono kapena chindoko. Koma maka maka matenda a masiku

210