28.07.2013 Views

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

anausunga ndikumvera konse monga mwa mau anu akuti 'Mwana wanga,

usaiwale malangizo angawa, koma mtima wako usunge malamulo anga'

(Miyambo 3:1). Tsono mutitsogolerebe pamene tikupitiriza mwambo wathu.

Amen.

Thank you Lord for guiding us through the fIrst part. Thank you for the testimonies of these

girls who have kept the counsel they were given according to your Word 'My child, do not

forget my teaching, but keep my commands in your heart' (Proverbs 3:1). Now we ask you

to lead us as we continue with our ceremony. Amen

Onse pamodzi ndi namwali aimirire kupanga bwalo nkumaimba nyimbo 1)'1 akubvina

mozungulira.

All, including the initiate, should stand and dance in a circle.

6. Yohanifotini, twenty wanii x 4

lye wondikonda ine x 4

Amvera lamulo langa

7. Popanda Mulungu kundikonda ine

Nkadakhala yanii lero?

Popanda Yesu kundisintha ine

Nkadakhala ndiri kuti lero?

John fourteen, twenty one x 4

One who loves me x 4

Obeys my command

Without God loving me

Who would I be today?

Without Jesus changing me

Where would I be today?

Onse atakhala pansi, mlangizi abwereze kufotokoza za chikondi cha Mulungu kwa ife mwa

Yesu Khristu, ifetu tiyenera kumumvera iye. Tiyenera kumvera malamulo ake chifukwa

timamukonda. Onse ayimbe nyimbo yotsatirayi polimbikitsa kuti pamene timvera Yesu, iye

adzatimangira mabanja athu, mpingo wathu, ngakhale mudzi wathu, ndi china chilli chonse.

While all are seated, one instructress should stress the fact that since God loved us through his Son, Jesus

Christ, we respond to his love by obeying God's commands. Sing the following song to emphasize that when

we obey Jesus, he will build our families, our church, our community, and so on.

8. Limanga banja 0 dzina la Yesu

Limanga banjaa dzina la Yesu

Limanga mpingo 0 dzina la Yesu

Limanga mpingoo dzina la Yesu

Limanga mudzi 0 dzina la Yesu

Limanga mudzii dzina la Yesu

It builds marriage 0 the name ofJesus

It builds marriagee the name ofJesus

It builds the church 0 the name ofJesus

It builds the church the name ofJesus

It builds society 0 the name ofJesus

It builds society the name ofJesus

Onse atakhala pansi, amayi awm asonyeze sewero lamtsikana amene wakula koma

akuganiza kuti waphweteka.

While all are seated two women act showing a girl who has matured but knows nothing about it and thinks that

she is hurt. She therefore tells her dad who takes her to the hospital.

Mtsikana: Adadi, taonani ine ndaphweteka, kaya ndi chiyani chandicheka!

Abambo: Aaa! Kodi mumasewera bwanji? Taonani tsopano waphweteka

eeh! Onani magazi! Tiyeni kuchipatala!

207

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!