28.07.2013 Views

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

Machembere ayenera kumawafupa atsikanawa pamene akuimba ndi kubvina.

The women should give monetary gifts to the girls as they dance.

4. Yeli ye/ele, tandiona mzako /ero

Yeli, nkakumana ndi amfumu, ye/ele!

Mpo mmagwada /ero ye/ele!

Mwambo wake ngomwewu, Yeli ye/ele!

Joy yaaa, look at me today

Joy, when 1 meet with the chief, yaaa!

1kneel down today yaaa!

It is the same counsel, Joy yaaa!

Mizere yachiwiri ndi chitatu ya nyimboyi kumasintha nkumachula zimene adasintha monga,

anzanga akandiputa, mpo simbwezera; nkaona agogo asinja, mpo mmawalandira; nkapita

kuchalichi, mpo mmasesa lero, and so on. Mtsikana aliyense adzilowa mbwalo kuchula

ndikusonyeza chomwe adasiyacho, monga kugwada, kusinja, ndi zina. Akatha apitilire

kuyimba nyimbo iyi:

Tanthauzo ndi lakuti, mwambo wake ndiomwewu umene tonse tinasinthikira khalidwe lathu

loipa kutsata labwino.

In the second and third lines, one girl at a time goes inside and mentions the thing she has changed from, such

as 'I do not pay back evil for evil;' 1 now help the elderly;' 1 now clean the church building;' and so on. They

should continue to sing the following song:

The meaning is that this is the counsel we all receive which changes us from bad behaviour to good conduct. It

is only Jesus who can change our bad behaviour.

5. Kodi n 'ndani adakusintha khalidwe?

Ndiye Yesu, ndiye Yesu yekha, Ye/ele!

Chikondi cha Yesu nchopambana, Ye/ele!

Yesu, Kh% /athu, tasintha ife, Ye/e/e!

Tidzamvera ndikukonda inu Yesu!

Ye/e/e! Ye/ele!

Who changed your behaviour?

It is Jesus, it is only Jesus, Yaaa

The love ofJesus is great, Yaaa!

Jesus, our Ancestor, we have changed!

We shall love and obey you, Jesus!

Yaa! Yaa!

Tanthauzo la nyimboyi ndi kuti anthu akuyamikira kusintha kwa khalidwe lamtsikanayu.

Yankho lake akuti popeza iye adasiya kuopa mizimu, lero akukonda Kholo lenileni, Yesu

Khristu amene akukangalika kumukondweretsa ndi kumumvera.

The meaning is that other people are admiring the girl's changed behaviour; the response is that it is because of

her moving from dread ofancestors to love ofThe Ancestor, Jesus Christ, that her concern is now to please and

obey him.

Potsiriza gawo limeneli payenera kukhala kupuma panthawi yochepa, pamene anthu amwe

chakumwa chimene chakonzedwa.

At break time some drinks are served.

Gawi lachiwiriri, amayi busa kapena mlangizi atsegule ndi pemphero lakuthokoza Mulungu:

The pastor's wife or one instructress should begin the second part with a prayer ofthanksgiving to God.

Zikomo Ambuye chifukwa chakutitsogolera gawo loyambali. Zikomo

chifukwa cha umboni wa atsikana awa amene atamva mwambo wanu,

206

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!