28.07.2013 Views

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

The night's ceremony may be as follows. (This is just oneexample of chinamwali. The instructresses should

come up with many songs and drama with words from the Scriptures to make the rite more meaningful and

interesting to the young women.)

Machemebere ayimbe nyimbo (ziwiri ngakhale zitatu) kuti namwali adziwe chimene anthu

abwerera, monga,

The women should sing two or three songs concerning the purpose for the vigil, such as,

1. M'Baibulo, m 'Baibulo

Muli mwambooo

M'Baibulo, m 'Baibulo

Muli mwalankhula

In the Bible, in the Bible

There is counsel

In the Bible, in the Bible

There is speaking

Machembere aziimba akumuzungulira mtsikana atakhala. Ena a amayiwo atanyamula

maBaibulo kumanja kwawo ndikumamusonyeza namwaliyo. Tanthauzo lake ndikuti

ulangizi umene apatsidwe tsikanayo ndiochokera m'Baibulo. Popeza baibulo ndi Mau a

Mulungu, ndipo Mulungu ndi amene adatilenga. Mwambo wa Mulungu ndiye wotiyenera

ife.

The women should be singing while going round in a circle with the initiate seated. Some of the women can

hold a Bible in their hands and show it to the initiate. The meaning is that their counsel is from the Word of

God, who is our Creator. It is God's counsel which we must follow.

2. Sinkadabweratu ine

Sinkadabweratu pano

Yandiendetsa mnkhole yakoyi

I would not have come me

I would not have come here

It is your menses that have made me walk

Mtsikana ali chikhalire ndi phungu wake pambali, onse adziimba atachita bwalo.

Azizungulira, koma ena atayerekeza kubvala mwele, koma osabvula zobvala zawo.

Atanthauza kuti onse abwera chifukwa cha mtsikana amene wakula. 'Tsopanotu walowa

mbungwe la anthu akulu. '

While the girl is seated with her tutors, the others should be dancing in a circle while wearing something like

the menses linen, but not actually taking offtheir clothes.

They should explain the meaning that 'now you are mature, you are no more a child!'

3. Mukatere, mukatere

Ndiko kukula kumeneku

What you have done, you have done

This is what maturity is

Zimene zikuchitika panOZl ndichifukwa chakuti mwakula ndipo mulandire mwambo

woyenera.

What is happening here is because you have now come ofage and you need to be instructed.

Tsopano ndi nthawi yakuti atsikana akale aperekere maumboni a khalidwe lawo kupyolera

mu nyimbo ndi kubvina. Popezatu iwo tsopano ndi anthu akhalidwe labwino kunyumba

kwawo, mmudzi, komanso kumpingo kwawo.

After singing and dancing, the older girls should take the floor. The aim is to give their testimonies through

songs and dancing that it is because they received the same teaching they are now good girls in their

community, in their homes, even at church.

205

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!