28.07.2013 Views

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

Ndi udindo wa alangizi kukonza maphunziro a atsikana onsewa kamodzi pamwezi.

It is the responsibility ofthe instructresses to arrange meeting with the girls once every month.

CHINAMWALl (KUTHA MSINKHU)

PUBERTY RITE CEREMONY

Malangizo kwa Alangizi

For the Instructresses

Pamene alangizi mwadziwitsidwa kuti mtsikana watha msinkhu, muyenera mukumane ndi

mtsikanayo mwansanga. Mumuuze mwachidule tanthauzo la zimene zamuchitikirazo.

Mumuphunzitsenso kabvalidwe ndi kasamalidwe ka mwele. Mtsikanayo asagwire ntchito

yolemetsa, komanso asayende yende mpaka atabvinidwa potsirizira pa msambowo.

When you have been informed that a girl has matured, you must meet with the girl as soon as possible. Briefly,

instruct her on the meaning of the menses, how to wear and take care ofthe linen. She must do light work and

should remain in seclusion until the chinamwali ceremony at the end ofher menses.

Muyenera kudziwitsa amayi busa anu amene adziwitsanso abusa. Dziwitsaninso

anamkungwi popeza ndiwo amene ayenera kukanena kwa mfumu. Mayi wa mtsikana

apereka nkhuku yokanenera kwa mfumu.

You must inform the pastor's wife who should inform the pastor. Inform also the traditional anamkungwi who

will inform the chief. The girl's mother must pay the chiefs dues.

Alangizi ndi mpingo, mogwirizana ndi makolo mukonzekere kumubvinira namwaliyo usiku

wonse potha pa msambo wakewo. Simba labwino ndi kunyumba kwa mlangizi, komabe

mukhoza kusankha malo ena opangira chinamwalicho. Alangizi, machembere a mumpingo,

makolo a mtsikana (osati mai ake), ndi atsikana olangizidwa kale a mumpingo (koma awiri

akhale aphungu), ayenera kudza kuchinamwalicho.

The instructresses and the church, together with the parents, should prepare for the night's vigil chinamwali at

the end of the girl's menses at the instructress' house, or any other house. The instructresses, the elderly

women ofthe church, the girl's aunt or grandmother, and the younger women ofthe church should be invited to

attend the chinamwali. Let two ofthem be tutors.

Anthu onse oitanidwawo atatha kudya chakudya chamadzulo pamodzi, abusa kapena akulu a

mpingo ayenera kutsegula mwarnbo ndi pemphero ndi mawu apang'ono achilimbikitso.

Chonde onenetsetsani kuti kuimba, kubvina, ndakatulo, ngakhale masewero, ziyenera

kutenga gawo lalikulu pachinamwali, kuti namwaliyo amvetse mwambo. Baibulo mukhoza

kuwerenga koma osati Bukhu la alangizi ayi.

When all the invited people have taken their evening meal, let the pastor or an elder begin with prayer and a

word ofexhortation from the vernacular Bible.

Please note that singing, dancing, and acting should be used in instructing the girl. You can use the Bible but

not the instructresses' booklet.

Mwambo wa usiku ukhoza kukhala motere. (Ichi ndi chitsanzo chimodzi, koma alangizi

muyenera kukonza nyimbo zambiri ngakhalenso maseweero ndi mau ochokera m'Bukhu

Loyera kuti chinamwali chikhale chopambana kwa namwali.)

204

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!