28.07.2013 Views

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

You must be committed to faithfully carry out the work God has entrusted to you. Inform your

congregation ifyou are unable to continue with ulangizi.

• Muyenera kukhala chitsanzo chabwino kwa atsikana ndi amayi anzanu pa umoyo

wanu wa tsiku ndi tsiku" kubanja kwanu ndi pakutumikira kwanu.

You must be exemplary to the girls and your fellow women in your daily life, in your family, and in

the way you serve God.

• Mukhale mai wophunzira mau a Mulungu ndi kupemphera nthawi zonse.

Be diligent in learning the Word ofGod and in prayer all the time.

• Khalani a luntha popanga nyimbo, ndakatulo, masewero, ndi zina zotere Zlmene

zingapangitse mwambo wa chinamwali chanu kukhala wopambana. Chinamwali

chizikhala mwambo wopambana ndi wosaiwalika kwa namwali wanu.

Be creative in coming up with songs, poems, drama, and so on. These are the things that make the

chinamwali ceremony to have a lasting impact on the initiate.

• Musawerenge kabukhu aka pamaso pa anamwali. Konzekani mokwana Zlmene

mukukalangiza. Ngati ndikotheka gawanani magawo pakati panu.

Do not read the booklet at the ceremony. You must prepare well in advance the things you are going

to counsel. Ifpossible, practise before and share the parts.

GAWO LACHIWIRI

SECOND PART

ATSlKANA OSATHA MSINKHU (ABUTHU)

PRE-PUBERTY INSTRUCTION

Pali zinthu zambiri zimene mtsikana amene sanathe msinkhu ayenera kuphunzira. Popeza

ntchito ya alangizi ndikuphunzitsanso atsikana njira ndi makhalidwe a Chikhristu, nthawi

yabwino ndi pamene sianathe msinkhu. Zina zimene atsikana ayenera kuphunzitsidwa ndi:

There are many things that a girl should learn even before puberty. One of the jobs of the instructresses is to

teach the girls the Christian way ofliving, and this stage is the best time to teach them. Some ofthe things that

the alangizi can teach the girls as follows:

Kudzisamala popewa chiwerewere

Taking care of herself by not indulging in sexual immorality

Kuchitira ulemu makolo, mafumu ndi akulu

Showing respect to the parents, chiefs, and the elders

Kumvera

Obedience

Kupewa maboza, kuba, ndi ndeu

Avoid lying, stealing, and fighting

Kukhala wolimbika pa kugwira ntchito kunyumba, mmudzi, ndi kumpingo

To be industrious at home, in society, and in the church

Kulimbika pakupembeza

To be diligent in attending worship services

203

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!