FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:
FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:
FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:
Create successful ePaper yourself
Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.
Gwiritsani ntchito ndime zalembedwa kotsirilizira kwa kabukhu aka pokambirana ndi

atsikana za chipulumutso chao. Alangizi ayenera kuwatsogolera atsikanawo kukula ndi

makhalidwe a chiKhristu, mpaka akalowe mbanja.

Teaching the girls the Christian way oflife. The instructresses should lead the girls who do not know Christ to

receive Jesus as their Lord and Saviour. They can use the verses which are at the back of this booklet. It is the

instructresses' responsibility to mature the girls in their faith until they are married.

2. Kulangiza. Alangizi ayenera kulangiza mtsikana pamene watha msinkhu; ayenera

kumulangiza mmene angakhalire ndi bwezi lake; amulangize paukwati wake, pamimba

yoyamba, ndi pamene mwana wabadwa. Alangizi ayeneranso kupitiriza kulangiza azimayi

magawo oSlyanaslyana.

Counsel. The instructresses should give appropriate counsel when a girl has matured, when she is dating

someone, on her wedding, at her fIrst pregnancy, and when the fIrst baby is born. The instructresses should

also give continuous counsel to the women in their congregation.

MAPHUNZIRO A ALANGIZI

TRAINING FOR THE INSTRUCTRESSES

Alangizi, monga anamkungwi, ayenera kukhala odziwa bwino ntchito yao. Chomwecho ndi

udindo wampingo kukonza maphunziro a alangizi pamene angosankhidwwa, komanso

nthawi ndi nthawi. Kawiri kawiri m'busa ndi mai busa ndi atsogoleri ena ayenera

kuphunztisa alangizi awo.

Atsogoleri a Association naonso ayenera kukonza maphunziro a alangizi kamodzi ngakhale

kawiri pachaka.

Like the anamkungwi, alangizi should know their work well. Therefore, it is the responsibility of every

congregation to arrange training sessions for her instructresses as soon as they are chosen, and from time to

time. Normally it is the pastor, or his wife, or other church elders who should conduct the training.

MAU KWA ALANGIZI ONSE

WORD TO ALL THE INSTRUCTRESSES

Ambuye akutsogolereni pamene mwabvomera kutumikira Ambuye mugawo la ulangizi iri!

Zinthu zina zimene muyenera kuzindikira ndi izi:

May God guide you in this ministry which you have accepted to do. Some ofthe things you need to know are:

• Musaziderere, Mulungu ndi amene wakusankhani, ndipo akuthandizani.

You should not undermine yourself. God is the one who has chosen you and he will help you.

• Onenetsetsani kuti mwalandira maphunziro a ulangizi pampingo panu, komanso

pitani kumaphunziro a Association a zaulangizi. Musayambe ntchito pamene

simunaphunzitsidwe.

Make sure that you have received the necessary training for your job. You must also attend the

Association's leadership training. Do not start to work when you have not been trained.

• Muyenera kudzipereka ndi kukhala wokhulupirika pantchito imene Mulungu

wakudalirani nayo. Dziwitsani mpingo ngati pali zifukwa zimene zikulepheretseni

kutumikira.

202