28.07.2013 Views

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

the first baby, as well as to all women. Since death is also a type of initiation, the church must prepare

appropriate instructions and teachings concerning death.

TISANKHE BWANJI ALANGIZI?

HOW TO CHOOSE ALANGIZI

Posankha alangizi, makolo amumpingomo ayenera kusankha amayi awiri, atatu, kapena

anayi amene akhala mumpingo zaka zisanu kapena kupitililapo ngati kuli kotheka. Ayenera

kukhala amayi okhulupirika ndiokula muuzimu, ndikuwonetsa zitsanzo zabwino

pamakhalidwe awo (Tito 2:3-5). Amayiwa akhoza kukhala pamabanja kapena ai, koma

ambiri yabwino. Alangizi asankhidwe chaka ndi chaka, kapena zaka ziwiri ziri zonse, ndipo

akale awiri kapena mmodzi ayenera kupitiriza pamodzi ndi alangizi osankhidwa atsopano.

When choosing alangizi, all parents in the congregation should choose two, three or four women who have

been members for five or more years if possible. Alangizi should be faithful and mature Christian women of

exemplary lifestyle (Titus 2:3-5). They can be married or not as long as they are of good repute. The alangizi

should be chosen every year or every two years, making sure there is an old one with the new ones.

UDINDO WA ALANGIZI

THE ROLE OF THE INSTRUCTRESSES

Ulangizi ndiwofunika kwambiri pakati pa anthu onse. Mwana ngakhale munthu wamkulu

kuti akhale wa makhalidwe abwino, ayenera kulangizidwa nthawi ndi nthawi. Tikayang'ana

muBukhu Lopatulika tiona kuti mwazaza ndi ulangizi wosiyana-siyana wokhudza munthu

mmene angakhalire ndi khalidwe labwino lokondweretsa Mulungu amene anamulenga. Mau

a Mulungu amati:

Malemba Oyera onse ndi Mulungu amene adawalembetsa mochita ngati

kuwauzira, ndipo amathandiza pakuphunzitsa choona, pakutsutsa zolakwa,

pakuwongola zokhota, ndi pakuphunzitsa anthu za kukhala olungama.

2 Timoteo 3:16

Counsel or advice is important for all people. For a young person or an adult to live well he or she must be

counselled all the time. Scripture is full of God's counsel on how people can live lives pleasing to God.

Scripture says:

All Scripture is God-breathed and is useful for teaching, rebuking, correcting and training in

righteousness.

2 Timothy 3:16

Alangizi ayenera kudziwa kuti iwo anasankhidwa ndi mpingo kugwira ntchito ya Mulungu.

Chomwecho ayenera kukhala ophunzira Mau a Mulungu nthawi zonse kuti akakhoze

kulangiza bwino. Ntchito ya alangizi iri pawiri motere:

The instructresses should realize that the congregation has chosen them to serve God. Therefore they must

study the Word of God all the time so that they are able to counsel properly. The role of the instructresses is

two-fold:

1. Kuphunzitsa atsikana njira ndi makhalidwe a Chikhristu. Alangizi ayenera kutsogolera

atsikana amene sadziwa Khristu kubvomereza lye monga Mbuye ndi Mpulumutsi wawo.

201

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!