28.07.2013 Views

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

Onse azibvina akugwira thupi lawo ndikusonyeza kumwamba kokhala Mzimu

Woyera.

They should be dancing while touching their bodies and pointing towards heaven where the Holy

Spirit is.

16. Mwendo, mwendo nkuyenda

Maso, maso nkupenyera

Chimodzimodzi, ziwalo zachinsinsi

Ntchito yake m 'banja

Leg, leg is for walking

Eyes, eyes are for looking

Similarly, private parts

Their job is in marriage

Amayiwo ayenera kusonyeza ntchito yake ya chiwalo chochulidwacho. Koma

akachula ziwalo za chinsinsi, azisonyeza pongodikhula mwaubwino. Ayenera

kumubvinitsanso namwaliyo.

Chiphunzitso chake ndi chomwecho chakudzisunga osadzidetsa mpaka adzakwatiwe.

Chiwalo chiri chonse chiyenera kugwiritsidwa ntchito molemekeza

Mulungu.

The women demonstrate the use of the part that is mentioned, such as leg for walking. But for the

private parts, they should demonstrate by shaking their waist up and down. They should let the

initiate dance also.

The teaching is still on sexual purity until marriage. Each part of the body should be used to honour

God.

Chiphunzitso chotsatirachi chipangidwe musewero. Ndilokhuza atsikana awm

kapena atatu amene akuphunzira kumachokera pakhomo pamakolo awo.

The following instruction should be acted by two to three girls who are day schooling and are

staying with their parents.

Atsikanawo akaweruka kusukulu, mmodzi amabwerera kunyumba, koma enawo

amayamba kucheza ndi anyamata nkumakafika mochedwa kunyumba. Makolo

awo akawafunsa amati amagwira ntchito yasukulu. Patapita nthawi, mmodzi

wapezeka ali ndi pakati nasiya sukulu. Mnyamata wake adaikana mimbayo.

Mtsikanayo anabvutika nayo mimbayo popezanso makolo amtsikanayo anaipidwa

nazo. Mwana atabadwa, mtsikanayo amangodwala dwala ndipo mayi wake

analibe nthawi yomuthandiza, popeza anali mayi wa bizinesi. Mtsikanayo amangosilira

mzake uja atatsiriza sukulu mpaka kumanga ukwati ku mpingo.

Kudwala kudapitirira mpaka kumwalira. Pamaliro anthu ankangonong'onezana

nkumati kodi si edzi imeneyi?

132

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!