28.07.2013 Views

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

Anamkungwi amuonetse mtsikana kabvalidwe ka mwele bwino-bwino. Amupatse

nayenso achite monga waonera mpakana akhonze ndipo anthu alulutire.

Amuonetsenso kachapidwe ndi kasungidwe kache pamene nyimbo ikuimbidwabe.

Potsiriza abwereze kumulongosolela kuti:

While still singing, the instructresses should demonstrate and teach her well how to wear the menses

linen and how to clean and take care ofthem. They should then explain the following to her:

Tsopanotu iye ayenera kudzisamalira thupi lake koposa kale. Akhale waukhondo

nthawi zonse ndi thupi ndi zobvala zake. Mtsikana adzisamalire kwenikweni thupi

lake ndi nsaru zake panthawi imene ali mumsambo kuti asapezeke akutulutsa

fungo loipa. Komanso asakhetsere paliponse mwazi wamsambo, popeza zimachititsa

manyazi kuti ena aone mwazi umenewu. Kuyimba kupitirire.

Now she must take care of her body more than before. She must keep her body

and her clothes clean at all times, particularly when she is menstruating so that no

bad smell comes out. She must make sure that no blood stains remain anywhere

for is it a shameful thing for people to see the stains. The singing continues.

12. Kumana, kumana mtsikana x 2

Mmati undipatse

Wabvundikira

13. Mulungu adawauza Adamu nda aHava

Muberekane, muchurukane

Refuse, refuse the girl

I wanted you to give me

You have covered

God told Adam and Eve

Be fruitful, and increase in number

Longosolani kuti njira imene amatipatsira ana Mulungu ndi yakugonana mwamuna

ndi mkazi amene ali pabanja. Kugonana kwa mwamuna ndi mkazi amene

sali pabanja ndi chimo la chigololo pamaso pa Mulungu ('Usachite chigololo'

Eksodo 20:14; 1 Akorinto 6:13,19).

They should explain that God gives us children through sexual activity in a marriage. Therefore

sex outside marriage is adultery to God ('Do not commit adultery' Exodus 20: 14; 1 Corinthians

6:13, 19).

14. Kodi lamulo la Mulungu likuti chiani?

Likuti Usachite chigololo

15. Kodi abale simudziwa eel

Simudziwaaa eel

Kodi abale simudziwa eel

Simudziwaa eel

Thupi lanu liri kachisi, liri kachisi

Wa Mzimu Woyeraaal

What does God's law say?

It says do not commit adultery

Friends, do you not know eh!

Do you not know eh!

Friends, do you not know eh

Do you not know eh!

Your body is a temple, is a temple

Ofthe Holy Spiritiii!

131

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!