FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:
FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:
FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:
You also want an ePaper? Increase the reach of your titles
YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.
9. Ndinu mudanlenga inetu eee!

Mudandiumba bwinotu eee!

Ntchito zanu zonse nzodabwitsa eee!

Onani lero ndakula

Ndakulatu, ndakulaa.

Akatha kubvina, amulongosolele mtsikana kuti:

You created me yaa!

You moulded me well yaa!

Your works are wonderful yaa!

Look today I have matured

I have matured, I have matured ye!

Mulungu adatilenga kuti thupi lamunthu likamakula limasinthika mumsinkhu ndi

mmaonekedwe. AkafIka msinkhu wina mtsikana amayamba kusamba kwa masiku

seven kapena kucheperako (kutuluka magazi kokozera). Kusambaku kumapitiria

kamodzi pamwezi. Chizindikiro chimenechi chimaoneka kwa akazi onse. Chomwecho

sizodetsa nkhawa kuti ndi matenda.

Kusambaku kumalozera zamtsogolo. Imeneyi ndi nJlra yomwe anakonza

Mulungu pofuna kutipatsa mphatso za ana.

Apitirize kuyimba,

After dancing the instructresses should give the following explanation to the girl:

God created us so that as we grow our bodies change both physically and in how we look. At a

certain point the girl begins to menstruate for about seven days or less (blood coming out of the

private parts). This blood flow happens once a month to all women. It is not any illness to worry

about. Menstruation foretells the future role. This is God's own way in order for us to have children.

They should continue singing,

1O.Mwateremu dzisamaleni a Joyce x 3

Bvalani mwele

11. Nchenje, nchenje, taona

Nchenje, yaonanji?

Yaona n 'nkhole

Now with this, take care ofyourself Joyce

Wear menses linen

Fly, fly, look

Fly, what has it seen

It has seen the menses

Kutanthauza kwa nyimboyi ndiye kuti namwaliyo adzidzisamalira maka akamasamba

kuopa kununkha.

The meaning of the song is that the girl should take care of herself whenever she is menstruating

so that she does not smell.

130