FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:
FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:
FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:
Create successful ePaper yourself
Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.
7. Papanda Mulungu kundikonda ine

Nkadakhala yanii lera

Papanda Yesu kundisintha ine

Nkadakhala ndiri kuti lera

Without God loving me

Who would I be today

Without Jesus changing me

Where would I be today

Onse atakhala pansi, mlangizi abwereze kufotokoza za chikondi cha Mulungu

kwa ife mwa Yesu Kristu, ifetu tiyenera kumumvera iye. Tiyenera kumvera

malamulo ake chifukwa timamukonda. Onse ayimbe nyimbo iyi kulimbikitsa kuti

pamene timvera Yesu, iye adzatimangira mabanja athu, mpingo wathu, ngakhale

mudzi wathu, ndi china chili chonse.

While all are seated, one instructress should stress the fact that since God loved us through his

Son, Jesus Christ, we return this love by obeying his commands. They should all sing the following

song to emphasize when we obey Jesus he will build our families, our church, our community,

and so on.

8. Limanga banja a dzina la Yesu

Limanga banjaa dzina la Yesu

Limanga mpinga a dzina la Yesu

Limanga mpingaa dzina la Yesu

Limanga mudzi a dzina la Yesu

Limanga mudzii dzina la Yesu

It builds marriage oh the name ofJesus

It builds marriagee the name ofJesus

It builds the church 0 the name ofJesus

It builds the church the name ofJesus

It builds society 0 the name ofJesus

It builds society the name ofJesus

Onse atakhala pansi, amayi awm asonyeze sewero lamtsikana amene wakula

koma akuganiza kuti waphweteka.

While all are seated two women act showing a girl who has matured but knows

nothing and thinks she is hurt. She therefore tells her dad who takes her to the

hospital.

Mtsikana: Adadi, taonani ine ndaphweteka, kaya ndi chiyani chandicheka!

Abambo: Aaa! Kodi mumasewera bwanji? Taonani tsopano waphweteka eeh!

Onani magazi! Tiyeni kuchipatala!

Anthu onse nkuseka. Ndipo anamkungwi aimirire nayambitse nyimbo (Masalimo

139:13-14):

Girl: Dad, look, I have hurt myself; I do not know what has cut me!

Father: 0, No! How do you play? Look now you have hurt yourself, eh! Look at the blood! Let's

go to the hospital!

They all laugh. Then the instructresses stand and begin to sing a song from Psalm 139: 13-14.

129