28.07.2013 Views

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

While the girl is seated with her tutors, the others should be dancing in a circle while wearing

something like the menses linen, but not actually taking offtheir clothes.

They should explain the meaning that 'now you are mature, you are no more a child!'

3. Mukatere, mukatere

Ndiko kukula kumeneku

What you have done, you have done

This is what maturity is

Zimene zikuchitika panozl ndichifukwa chakuti mwakula ndipo mulandire

mwambo woyenera.

What is happening here is because you have now come ofage and you need to be instructed.

Tsopano ndi nthawi yakuti atsikana akale aperekere maumboni a khalidwe lawo

kupyolera mu nyimbo ndi kubvina. Popezatu iwo tsopano ndi anthu akhalidwe

labwino kunyumba kwawo, m'mudzi, komanso kumpingo kwawo.

After singing and dancing, the older girls should take the floor. The aim is to give their testimonies

through songs and dancing that it is because they received the same teaching they are now good

girls in their community, in their homes, even at church.

Machembere ayenera kumawafupa atsikanawa pamene akuimba ndi kubvina.

The women should give money gifts to the girls as they dance.

4. Yeti yelele, tandiona mzako lero

Yeti, nkakumana ndi amfumu, yelele!

Mpo mmagwada lero yelele!

Mwambo wake ngomwewu, Yeti yelele!

Joy yaaa, look at me today

Joy, when I meet with the chief, yaaa!

I kneel down today yaaa!

It is the same counsel, Joy yaaa!

Mizere yachiwiri ndi chitatu ya nyimboyi kumasintha nkumachula zimene adasintha

monga, anzanga akandiputa, mpo simbwezera; nkaona agogo asinja, mpo

mmawalandira; nkapita kutchalichi, mpo mmasesa lero, ndi zina. Akatha apitilire

kuyimba nyimbo iyi:

Tanthauzo ndi lakuti, mwambo wake ndiomwewu umene tonse tinasinthira

khalidwe lathu loipa kutsata labwino. Ndi Yesu yekha angasinthe munthu kukhala

wakhalidwe labwino.

In the second and third lines, one girl at a time goes inside and mentions the thing she has changed

from, such as 'I do not pay back evil for evil,' 'I now help the elderly;' 'I now clean the church

building;' and so on. They should continue to sing the following song:

127

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!