28.07.2013 Views

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

SHOW MORE
SHOW LESS

You also want an ePaper? Increase the reach of your titles

YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.

Please note that singing, dancing, and acting should be used in instructing the girl. You can use the

Bible but not the instructresses' booklet.

Mwambo wa usiku ukhoza kukhala motere. Ichi ndi chitsanzo chimodzi, koma

alangizi muyenera kukonza nyimbo zambiri ngakhalenso masewero ndi mau

ochokera mBukhu Loyera kuti chinamwali chikhale chopambana kwa namwali

(anamwali).

The night's programme may be as follows. This is just one example of chinamwali. The instructresses

should come up with many songs and drama with words from the Scripture to make the rite

more meaningful and interesting to the girls.

Machembere ayimbe nyimbo (ziwiri ngakhale zitatu) kuti namwali adziwe

chimene anthu abwerera, monga,

The women should sing two or three songs concerning the purpose for the vigil, such as,

1. M'Baibulo, m 'Baibulo

Muli mwambooo

M'Baibulo, m 'Baibulo

Muli mwalankhula

In the Bible, in the Bible

There is counsel

In the Bible, in the Bible

There is speaking

Machembere aziimba akumuzungulira mtsikana atakhala. Ena a amayiwo atanyamula

maBaibulo kumanja kwawo. Tanthauzo lake ndikuti ulangizi umene

apatsidwe tsikanayo ndiochokera m'Baibulo. Popeza baibulo ndi Mau a Mulungu,

ndipo Mulungu ndi amene adatilenga. Mwambo wa Mulungu ndiye wotiyenera

ife.

The women should be singing while going round in a circle with the initiate seated. Some of the

women can hold a Chichewa Bible in their hands. They show it to the initiate. The meaning is that

their counsel is from the Word of God, who is our Creator. It is God's counsel which we must

follow.

2. Sinkadabweratu ine

Sinkadabweratu pano

Yandiendetsa mnkhole yakoyi

I would not have come here

I would not have come here

It is your menses that have made me walk

Mtsikana ali chikhalire ndi phungu wake pambali, onse adziimba atachita bwalo.

Azizungulira, koma ena atayerekeza kubvala mwele, koma osabvula zobvala

zawo.

Atanthauza kuti onse abwera chifukwa cha mtsikana amene wakula. 'Tsopanotu

walowa mbungwe la anthu akulu.'

126

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!