28.07.2013 Views

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

FROM CHINAMWALI TO CHILANGIZO:

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

When you have been informed that a girl has matured, you must meet with the girl as soon as possible.

Briefly, instruct her on the meaning of the menses, how to wear and take care of the linen.

She must do light work and should remain in seclusion until the chinamwali ceremony at the end

ofher menses.

Muyenera kudziwitsa mai busa anu amene adziwitsenso abusa. Dziwitsaninso

anamkungwi popeza ndiwo amene ayenera kukanena kwa mfumu. Mayi wa

mtsikana apereka nkhuku yokanenera kwa mfumu.

You must inform the pastor's wife who should inform the pastor. Inform also the traditional

anamkungwi who will inform the chief. The girl's mother must pay the chiefs dues.

Alangizi ndi mpingo, mogwirizana ndi makolo mukonzekere kumubvinira

namwaliyo usiku wonse potha pa msambo wakewo. Tsimba labwino ndi

kunyumba kwa mlangizi, komabe mukhoza kusankha malo ena opangira chinamwalicho.

Alangizi, machembere a mumpingo, makolo a mtsikana (osati mai

ake), ndi atsikana olangizidwa kale a mpingo (koma awiri akhale phungu), ayenera

kudza kuchinamwalicho.

The instructresses and the church, together with the parents, should prepare for the night's vigil

chinamwali at the end of the girl's menses at the instructress' house, or any other house. The

instructresses, the elderly women of the church, the girl's aunt or grandmother, and older girls of

the church who have been through the rite should be invited to attend the chinamwali. Let two of

the girls act as tutors.

Anthu onse oitanidwawo atatha kudya chakudya chamadzulo pamodzi, abusa

kapena akulu a mpingo ayenera kutsegu1a mwambo ndi pemphero ndi mawu

apang'ono achilimbikitso kuchokera m'Bukhu Lopatulika. Monga mau ochokera

pa Genesis 1:26 'Tipange munthu muchifanizo chathu, monga mwa chikhalidwe

chathu.' Apemphere kuthokoza Mulungu chifukwa chakulenga munthu mu chifanizo

ndi chikhalidwe chake. Apempherenso kuti Mulungu awateteze amayi ndi

anamwali onse pa mwambo umenewu.

When all the invited people have taken their evening meal, the ceremony should begin by prayer

and a word of exhortation from the pastor or an elder. He can give an exhortation from Genesis

1:26 'Let us make man in our image, in our likeness' and pray thanking God that he created us to

be and live like him. Also asking God to protect the women and the initiates from all dangers during

the ceremony.

Kuimba, kubvina, ndakatulo, ngakhale masewero, ziyenera kutenga gawo lalikulu

pachinamwali, kuti namwaliyo amvetse mwambo. Baibulo mukhoza kuwerenga

koma osati Bukhu la alangizi ayi.

125

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!